Email a copy of 'China ‘commodity aid’ for Malawi: Donate Police vehicles' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'China ‘commodity aid’ for Malawi: Donate Police vehicles' to a friend
Scotland's former First Minister Lord Jack McConnel has hailed the existing coordial relationship between Malawi and Scotland which dates back...
Pakatha chaka chimodzi muzizati ndalama zina Tagura magalimoto ku CHINA..ngati mwachitira ndi stadium(Bingu national stadium) munabwera koyamba munati achina atithandiza ndi stadium,kachiwiri munasitha muli ndi ngongore ya 20b tizibweza pang’onopang’ono for 20years amanga mastadium awiri pano nde mukuti ndalama zomwe zapita ku Sports pa budget akufuna amalizile stadium(Bingu national stadium,chenicheni ndi chiti?mukangopanganso ndimangalimotowa Tizamacha!!komanso kodi Galimoto imeneyi mukuti kukhazikisa chitetezo kodi ndi nkhondo kapena chani?mukufuna muzitipha tikamakuzuzulani ndi ziwonesero?
Inu Matchalenizi Nanga Chimanga Simugawa? Chaka Chino Kulibe Chakudya Chokwanira
basi kusangalala kumakambilana za donation.pangani za malipilo a wanthu,amalawi anakakhala mankhwala bola magalimoto,mumalephela kuthamangitsa mbala nkumati mulibe fuel,kapena izo ndizoyendela mikozo
Can’t you pls donate us with mabomba atimkenawo?,cox kumalawi kuno nde zafika pa worse tsopano,kuyambira zachuma,zamaufulu,zandale nde nanji!,mabombawo mwina akanatithandiza kupanga restore dziko lino,ndakwiya nanu nanu atsogoleri adwera inu!,stuped zanu!!
Thanks 4 the gift,i hope everything will endup well,coz MW is the peace country….
THE VEHICLE ON THE PICTURE IS JUST A SAMPLE AND BELONGS TO MALAWI POLICE. ITS NOT ONE OF THE VEHICLES FROM CHINA. THE CHINESE CONSIGNMENT IS YET TO ARRIVA IN THE COUNTRY. UMBULI BASI!
OTHER SO CALLED DONORS MUST EMULATE THE CHINESE! DONT YOU SEE WHAT CHINA IS DOING.
Mtipatsekoso mifit ndi ma bomba. Bola osadzatikumba…….
Point of correction,
China sichimachita donate, TIZAPEREKA NDALAMA NDITHU, NDI NGONGOLE IYI.
Malawian we must obey chinese government for helping to archive development in a country,koma sitimva kuti aba magalimoto azikanyamulira zokolora