Email a copy of 'Chisomo Machero is new Miss Blantyre: Malawi Poly student' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

60 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Enock Gideon
8 years ago

koma abale bola munakatengatu kwa mayaka anthu akumudzi enieni akanawina zimenezi. koma awa ndiye iiiiiiiiiiiiiiiiiiii, Miss or Mr ? khope ngati amuna , Dkaka ndiy kutali kwenikweni wazaka 34 mukuti 20, wa 29 mukuti 19 ndipo wa zaka 36 mukuti 21 . whats that?

general mwalala
general mwalala
8 years ago

makosana dzuwa salozerana aliyense amaliwona yekha. kodi awa ndi anthu kapena Zombie kapena titi Dzombe. zaka mwachosera, makholo ngatitu amenewa akakhale ndi zaka 19, 20 and 21?? basi kuyambira lero dzina la Blantyre latha and u should go back to your former name: Kabula. nyasizi Ife ayi

KAMBWE
8 years ago

IWE Dan ngwira zoona kukhala chairman wa organising committee ..kusankha mzukwa ngati uwu..kungomva ngwaku Poly eti …anakuonesa ntchafu kaye kapena..

KAMBWE
8 years ago

IWE Dan ngwira zoona kukhala chaiman wa organising committee ..kusankha mzukwa ngati uwu..kungomva ngwaku Poly eti …anakuonesa ntchafu kaye kapena..

Real African
Real African
8 years ago

Koma Blantyre inatha. Ameneyu mungamati mIss Blantyre? Atsikana kulibe? Inu Mbuzi eti?

professor goodwell
professor goodwell
8 years ago

sindikuwonapo mkazi apa,nkhwangwa ngati imeneyi nkumala Miss Bt?Chinyengo basi

sigweje
8 years ago

mbewa zikatha anona ndi aswiswiri.izitu mzotseketsa okumwa ma ARV ndi odwala ebola.

malawi
malawi
8 years ago

hahahahaha 1st first princes

John Blantyre
John Blantyre
8 years ago

iyi ndi mizukwaka kodi????????????????? lets be real ndi ma model opanga encourage to contest this is an embarrassment to the malawian ladies and abomination to the blantyre community………….HOLY GHOST FIRE!!!!

Vikunowa
Vikunowa
8 years ago

Hhhh bodza true represenattionya ma babie apa BT ameneyo ndi Mis BT zeni zeni. Watch this space for Miss LL otsikana opaKasiya osati zanuzi. ha ha ha ha ha ndakusekani anthu aku BT

Read previous post:
DPP says MCP’s fears of Speaker impeachment ‘unfounded’

The governing Democratic Progressive Party (DPP) has dismissed as “unfounded” fears by, the Malawi Congress Party (MCP) that government has...

Close