Email a copy of 'Chiukepo inspires Nyasa BB win against Epac: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chiukepo inspires Nyasa BB win against Epac: Malawi TNM Super League' to a friend
Bishop for Karonga Diocese of the Catholic Church Martin Mtumbuka has said people who steal church offering of plunder church’s...
Nyasa dubious penalties Ulesi…kukhalira kubelekedwa basi…
LINDANI MADZI APITE. CHAKA CHINO NDI CHA NYERERE BASI. TIDAKUTURUKIRANI. MUMADALIRA A REF KUTI AKUPATSENI PENALTY. If BB fails to score a genuine goal, the ref is ready to come to their rescue. How many free penalties have you been offered? Ingotini phee muwone. Chaka chino muwona bwadza. Sindidazione adachezera ndi kuziona.
ndichifukwa Chake Feremuzi siichita bwino,aChiukepo zimawanyera kuchinya ku Theba lero asanduka dolo pa nyasalande!Malawi wanga uneeee
Maulee ndi maulee basi
Ana achepa. Maule ndi more!
Well done Maule.Mwatimvetsa kukoma. Pitilizani kupambana ndipo timakunyandirani. Kaya zivute or zisavute tili pambuyo panu basi NGANGANGA.Kuno ku Phalombe
Ndiyo yake a Headmaster STD 3B i like that
Maule Kupitiliza Pomwe Tinasiila,blue Eagles Fans Take Care ,we Are Coming To Take Our Bag Of Money.Ndizandalama Izi.Sitinalowe Mu League Kudzasewela Kapena Kudzacheza
Koma luso loti Ukachinya iweyo anzako asachinyeso nde zopusazo. Ngati ndi zithumwa ukabwenze,luso ulinalo kale.