Mpaka silverkufuna chiukepo, ine kumva kukoma ndi mapale anga. Chaka chino quadruple basi
TOBACCO
8 years ago
KODI ACHIUKEPO ANAPHWISIRA NDI NDANI PAMBIRI YA MALAWI PALIBE PLAYER KUPOSA CHIUKEPO AMENE WAPITA MA TRIALS AMBIRI KOMA KUMANGOTI DIKILA KAYE CHILIPO CHINACHITIKA KOMA NDITHU
Wakufa sakudziwika mind you this is another yr everybody has reviewed his fomula so take care
we are grad as bullets to have him back watch out other teams we will take avery trophy this season and watch nice passing football
Chiukepo kaya walephera kaya watani enanu sizikukukhudzani pangani za matimu anu,msanje bwanji?
osatinamizapo apa,Chiukepo zamukanika bas,sadzaiphulaso ameneyu
this is the year big bullets will destroy and kubata pasi tumatimu tunyake tonse….mubwefulikenge namatumbu fulumu
The truth is…he has failed the trials…don’t beat about the bush
Mpaka silverkufuna chiukepo, ine kumva kukoma ndi mapale anga. Chaka chino quadruple basi
KODI ACHIUKEPO ANAPHWISIRA NDI NDANI PAMBIRI YA MALAWI PALIBE PLAYER KUPOSA CHIUKEPO AMENE WAPITA MA TRIALS AMBIRI KOMA KUMANGOTI DIKILA KAYE CHILIPO CHINACHITIKA KOMA NDITHU
Wina aona ukweche.neba wagenda katauluka kkkk.
Zili bwino ndipo wina alira