Email a copy of 'Cholera outbreak strikes Malawi: One death, 26 cases confirmed in Machinga, Zomba' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Cholera outbreak strikes Malawi: One death, 26 cases confirmed in Machinga, Zomba' to a friend
Prophet Shepherd Bushiri told congregants at this Enlightened Christian Gathering (ECG) in South Africa to see live the Angels appearing...
Kodi mukuti boma litani?lipite ku Chirwa lizikawasambira mmanja,kuwapitiraku toilet ndikuwatsukila mango anthuwa?
What stupid policies are you talking about?
What have you personally done to make your rural relatives understand the importance of personal hygiene or having a latrine
Guys ukhondo ndiofunika osamangodya mango osatsuka
Ine dziko lino landikwana.Malawi pakana lero kulimbanabe ndi cholera? Dziko lotemberedwa ngati ili sindinalione padziko lapansi.Tunalakwa chiyani
Its a combination of so many factors. We are too many to be contained in a small country like this and we got stupid policies on everything.
This lake will kill all of us one day while Ministry of health know that it is the source of Cholera. Where are epidemiologist and public health experts in this ministry of hell!!!? What health if not hell? Who is the director of preventive health? Tell him go to hell stupid man
Eeeeeeeeee koma chonde,,,,,ambuye tichitireni chifundo,,,,,,,,zisafike povuta dere kuzomba kuno
kupepera kwenikweni zaka 55 tikuvutika ndi nthenda imodzi modzi simungachitepo kena kake ai koma zikavuta ndiye muziti we are doing everything possible
Eeeee kufunika kusamala amalawi.matenda awa ndiwopeweka ndithu,bola kuwonetsetsa kamwedwe ndikadyedwe ka zithu zomwe tilinazo m’manja mwathu. Malawi be careful.
very sad indeed.