Email a copy of 'Civil servants salary increase remains 24% -Malawi zero-aid budget' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

33 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
pooooopo
9 years ago

Guys, zinalakwika ndi previous government. Mumvesese kuti this is ZERO AID budget chifukwa cha cashgateeeee!!!! ok chabwino basi boma lingolamula aliyense azipereka pa chaka 2000 kwacha kuti boma lipeze ndalama zokuonjezerani malipilozo, musangalala? nde mukuti boma likatenge kuti ndalama? likakweza ma feez azinthu zina ndi zina mukutiso boma lalakwa? nde litani bomalo? this is the best the government can offer pliz. Iam a CIVIL SERVANT my self koma ndikutha kumvesa. Khalani ndi umunthu guys. Musalowesepo ndale apa. This year ndi yovuta. Next year it will be another increment. Things are not ok economically in Malawi so boma lili pa pressure.… Read more »

Mam nyox
9 years ago

mudzadziwa kuti nyau mmunthu 2019.mudzatifuna alomwe ,agalu inu

peter
peter
9 years ago

You Policemen you were saying chala m’mwamba ndizimezotu mukulira chiani? Mukhaula. 24% basi yakwan imeneyo . muzigona nyumba ngati ndendezo basi simungamange nyumba olo ya a mai anu kumudzi kwanu munya muona. Paja mumabvina kuti Mathanyula wawina mukhaula. Nanga uniformu ija amakuudzani kuti akugulirani nthawi ya kampeni iri kuti? Mabanja anu ntchito kugulisa kanyenya m’mbali mwamseu ndi thobwa zomvetsa chisoni Nyumba zanu za chipinda chimodzi basi. Nanga lero mukuliriranji? 24% basi kwainu apolisi. Bola Mai aja amakupasani thumba la chimanga . nanga mathanyula ali ndi munda?

Jordan Chikoti
Jordan Chikoti
9 years ago

please motivate the civil service with atleast a 60% salary increment since they are doing a very recomendable job.

Umunthu
Umunthu
9 years ago

Where are you Elijah Kamphinda Banda? Mukadakhalapo Dr Kamphinda Banda, we would have won this battle. But these guys you left, are yet to help us. Kodi mumakasankhirana kuti?

Concerned citizen
9 years ago

Count your self highly favored to have gotten such a good increase.

okwiya ku makanjira
okwiya ku makanjira
9 years ago

zili bwino anthu tinavotera ngati tayiwala boma limeneli litichangamutse kuti 2019 tizasankhe mwanzeru

godobaman
godobaman
9 years ago

mfiti sikudya maliro kokha koma zomwe akuchita a DPP ndi ufiti ndithu wapadera

Cutbert Kamanga
Cutbert Kamanga
9 years ago

Munawombera nfiti manja.a polisi ndi teachers r fools.u made ths nyau to win:mukulira chani?shupiti:mukanali kukhalira katapila:agalu inu!

GADABWALI
GADABWALI
9 years ago

You promised us SADC salaries, is this wat u meant? Sitiyiwala, mudzatifuna agalu inu.

Read previous post:
Malawi reduces new HIV infections

Malawi has managed to reduce new HIV infections with current figures indicate that new infections now stands at 35,000 per...

Close