Email a copy of 'Civo bitter with Nyasa Bullets ‘poaching’ players : Battle over Zoya, Lanjesi' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

11 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
paul ck banda
paul ck banda
8 years ago

zilibwino kwambili

Jackson yohane
Jackson yohane
8 years ago

Kunena zoona Bullets yalakwitsa koma asiyeni basi atenge maplayerwo chifukwa ndiye kuti agwilizana nazo zonse

Madalitso mmangitsa
Madalitso mmangitsa
8 years ago

Asiyeni akasewele ku the pples team ndondomeko isatidwa mulandila zomwe mukufunazo

Buyelekhaya
Buyelekhaya
8 years ago

Chingambwe money is driving some people mad. Fisi ndi fisi!

sir bentry chillwar
8 years ago

BULLETS approached #Civo for two
players; Lanjesi and Zoya. Then Civo
named their price (4 million each) and
today,Bullets unveiled them! What does
that mean? Simple logic! It means Bullets
has agreed to pay the amount,as simple
as that!!!

Elder Soccer A15
Elder Soccer A15
8 years ago

Thats why Malawi is going down in all sectors, busy defending law breakers, justifying wrong doing. It doesnot matter whether they are super league champions, they should follow the rules. Look at Kaizer Chiefs, Barca (Barcelona), Chelsea etc they follow transfer rules. This is why Gaba Mhango was fired from Celtic in South Africa. Dongosolo is important whether you are Messi, Yaya Toure, Gaba, or Zoya. Dunderheads!!!

Kabwafu fc chief supporter

Inde si anawo,ali ndi makolo awo omwe anawabeleka;komano za mpila izi ndipo zimakhala ndimalamulo ake omwe anakhazikitsidwa; si mpila wa makwalala oti player amangodzuka lero ndi lero ‘ndasiya team yanu guys’ ayi sizilichoncho izi; nde bullets ikuyenera kutsata dongosolo kut ma player wo akhale a team yawo, eeetu!

Hawkins chiwaya
8 years ago

Amenda leave the players to go atola chikwama amenewo. Bb ndi supper league champions alipo amene safuna kusewera mu team yamachampions ndani? Si ana anuamenewo munabereka ndi inuyo

Nyasa
Nyasa
8 years ago

kodi ndi player uti yemwe safuna atasewelera team ya Nyasa BB MENE ZATELEMU MUNGOZIWIRATU KUTI ANYAMATA AMENEWA APITA BASI MUZINGODIKIRA NDALAMA ZANU MULANDIRE BASI

kaluga
kaluga
8 years ago

A Mwenda khalani chete, osawaphela ufulu ma players,after all they are all grown up and can make their own decision

Read previous post:
Malawi can count on ‘reliable’ China for economic independence- Foreign Minister

As Malawi is facing slowing economy with commodities tanking due to continued aid freeze by Western donors,  China has given...

Close