Email a copy of 'Civo wins Standard Bank Cup final against Wanderers' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

58 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
yip
yip
8 years ago

NEBA mutu sukugwira

devilsadvocate
devilsadvocate
8 years ago

Did you guys get a credit note for the hired bus, since things didn’t go well? Pepa neba.

ntha.....
ntha.....
8 years ago

Neba… mutu siukugwira.

Hardson
8 years ago

Limbani limbani mitima a ulendo limbani limbani mitima. Pepa neba inenso zandiwawa ngakhala anthu osadziwa mpira anasokosa ku ofesi civo itakuntha timu ya fuko koma anthu a mtendere tinangoti chete panonso tili chete. Moti tikulira nanu limodzi. Wina walankhula za mwano kumati tiwine lig tibweze ngongole-awa ndi anthu amene amalankhula asanaganize koma asanafufuze kuti kulinji choncho ife sitikudandaula. Anthu amati a Bullets ndife aphokoso adabwa okha ife tili cheteee ngakhale nkhuku za noma za ku ofesi kwathu zinali dzyolidzyoli kuona ngati tibweza kulalata we are very decent and smart. Ndimakumbukira vesi la mBaibulo ngakhale sindikuyenera kutero komabe 1 Akorinto 5:5… Read more »

Victor
Victor
8 years ago

Pepani Neba masiku sakoma onse Basi limbikirani League mukhoza kuyiwina malinga muwine magame onse zikomo congrats Civo mwachotsa manyazi LL Zikomo masapota onse povomereza kuluza tiyene tipitirize kuti mpira upite patsogolo mwina mawa Flames ndikuyamba kuwina magame

Oscar D. Mulenga
Oscar D. Mulenga
8 years ago

Paja tinkanena kuti wina alira aeeee! Eeeeee! waliradiiiii!!!!!!! Kuzitama sikwabwino. Davide anapha Goliati. Cup Specialist ndiye kuti chiyani? Mutenge phunziro apa ‘Nyerere’ lero simwafa ndi dzuwa osati doom ayi

William Tembo
William Tembo
8 years ago

Guyz mwachita bwino kupha mbuzi zimenezi,zikanati nyansa mumzinda muno.

cbk
cbk
8 years ago

manoma osadanda,ya gate collection ndi runners up IJA yambiri.Neba wapindula chani?Uwine league tu ubweze ngongole IJA,apo bii akulanda basi anakupasa a tcheya IJA.

Klein
Klein
8 years ago

Munyanya manoma kuyakhura kwambiri titenga ma cup onse awiri?

Nya BB
Nya BB
8 years ago

Chalaka Bakha Nkhuku singatole kkkkkkkk maule palibenso

Read previous post:
Dave Banda receives 3rd red card as KB beat Epac 2-1

Kamuzu Barracks and former Flames international midfielder Dave Banda has made a record of his own by becoming the first...

Close