Email a copy of 'Clubs to suffer as Malawi coach clings to players' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

8 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Keen Observer
8 years ago

Most of the leagues around the globe are off season WHY our league is in progress? What calendar do we use?

Adam christon Masamba
Adam christon Masamba
8 years ago

!Lero zaipa pati? Maplayers anu ayitanidwa ku national team pano mukuti akutengerani maplayers oti, asewere mspl. Kodi mayesa kuti chani? Nanga tangoganizani ife nthawi ija; pamene maplayers athu, anayitanidwa kt akatumikire m’cosafa, inu kumasangalala kti, yaa.. Maplayers odaliliri aja achokapo, ndipo BB iyamba kumaluza. Km ayii, sizinatheke, bwanji pamenepo? Lero chagwera iwe,,,sunasewere nkomwe pano wayamba kale kulira. Iiiiiii!!! mayo oooo!! BB is my team of my heart.

Wawa phiri
Wawa phiri
8 years ago

Zatikhudza kwambiri ife Manoma, zatiwawa mumve.

LIZULU
LIZULU
8 years ago

IFE TIMAPANGA MA DRAW MA PLAYER ALI KU COSAFA MUMAYESA OPUSA? MUSOVA.BB MORE FIRE!!!!!!!!

James mkoko
James mkoko
8 years ago

Game sinamenyedwe mwayamba kale kulongolola nanga akaluza alekeni anawo awonetse lunso lawo kuti angule malo.

myao
myao
8 years ago

Zanga phee. Will be crossing paths but not hard feelings.iwe umafuna a Chancy ayambe u shehe kapena? Mesa flames ikufuna anthu opemphera, ulaliki pa half tym kkk

SOOTH SAYER!
8 years ago

FAM DOESNT OWN PLAYERS DERE4 OUR PLAYERS MUST BE RELEASED! ENERST AND CHANCE R BB SUPPORTERS! DATS FOUL PLAY!

zanga phee
zanga phee
8 years ago

sizikukhuzana, imeneyo ndi friendly game but we are looking for Points BABA,
you can use anyone apart from those who are playing their league games.
osamakhomelerana, musaiwale kuti player akavulala ku National team amavutika ndi ma club ndi makolo ake kumusamalira.
mukangoluza freandily imeneyi nonse wautali ndi a Chancy anuwo.
kani mmayesa anayamba zaubusa???????????????????????kkkkkkkk.

Read previous post:
Malawi High Commission in South Africa to celebrate 51st independence July 4

Malawi High Commission in South Africa is inviting Malawians who reside in South Africa and other nationalities to the interdenominational...

Close