Email a copy of 'Consortium demands Malawi jet probe outcome' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

58 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
chadza kwayani
8 years ago

Ngati mwasowa chochita pitani Ku chimbudzi mukaphwrtse n’khuto

Nyipi
8 years ago

Mukumatipusitsa choona mukuchidziwa. Ndalama za ndegezo adya nawo, that’s why akumachedwa kutiuza zoona zake. Onsewo ndi mbava. Palibe chipani chomwe chidzalamulire boma osaba. Dyera lakula!!!

Gwamula
Gwamula
8 years ago

The then Officers in the Jet gate are around, who needs the information, the then Minister can provide the information, we have the ODPP, we have in country retired army officers, we have active army officers who saw the Jet off. This attitude of Plato devil’s advocate its not own. You mean this DPP government failed to track the jet sale. Its a joke by this youth organisation that seem to be playing devi’s advocate!

Phwado
Phwado
8 years ago

Zayambika, tiyeni nawo anamachende ndi anamabumbuwa.Tiotche basi zitsiluzi!Boma likuchedwa chifuwa onse ndi mbava.Tigwire tokha mfitizi.More fire.

nicca
8 years ago

kodi mukufunanso amai asinthe maganizo angolengeza kumene kuti akubwera mwayambapo za ndege, kodi mmesa amma ananena kut ndalama iwo anagulira chimanga kut ana amalawi asafe ndi njala afotokoze bwa nji amma

Kanyimbi
Kanyimbi
8 years ago

za ziii basi. Mukumatumana kuti mutipusitse.

Sopo Walala
Sopo Walala
8 years ago

Achinyata Anzeru Inu, Mukufuna Mudziwe Za Ndege, Osati Zitsiru Zimati Zikasuta Chamba Zimangotukwana President, Zamkutu. More Fire

emmah
emmah
8 years ago

Koma ndi zoona tikufunardi Ife amalawi tidziewe kuti ndalama zake zinapita kuti chifukwa boma lapita linali kuba kwambiri mopanda chison chonde pano anthu akusoweka ndalama anabaiba kodi akadapanda ndalama akanakhala kunja amai amenewa ndiye mbava nambala wani chonde Nlama za ndege zioneke basi

blessing saizi
blessing saizi
8 years ago

My friend which stupid youths are you mobilizing? Ma youths apano amadziwa kukasaka money not all of us are like you a bunch of rotten bananas funded by disgruntled politicians to try and claim what does not belong to you. Fools!

sapitwa
sapitwa
8 years ago

The Youth are exercising their Democratic Right about the Jet and nothing else. They must be heard. Osawaphatikizira zina ai. Iwo akuti ndege osati Njaunju, or K92b or K577b ai. Ndege basi, zinazo mukufuna ndi inu, funsani nokha.

Read previous post:
Zodiak yet to apologise to Malawi President Mutharika

Private electronic media group, Zodiak Broadcasting Station (ZBS) is yet to apologise to President Peter Mutharika exactly a week after...

Close