To be honest most people listen to his (gondwa) commentry than uyu mukuti khalakaleyo. kodi mukufuna kumakhomerera achinyamatafe bwanji? he deserve it. if not satisfied listen to him next season
bbsupporter
9 years ago
Iweukuziti Chokazingawekunenerera mpira mu chichewa sikuti asapambane ayi. Ndiwe MBULI wamva? Botswana,South Africa,Mozambique unamva akunenelera mpira m’chizungu? Ku UK unamva akunenelere mpira mu Chichewa? Ndiwe GULO.
Kodi Gondwau akapose mikoko yogona wayamba liti unenelela mpira ine ata sindidziwa ndipang’ono pomwe ai pafunika kufufuza bwino mungaphe tsogolo lankhalakale chifukwa azichita ulesi
Pastand
9 years ago
Abale zafika Best Commentator ku Mpira mphoto zakutiko timaziwa ife ndi Best Presenter and Reporter where are these awards are coming from iwe Tiya sitikufunanso ku Mpira
mwasowa chonamizila. Dangerman has got a touch simanngo simango what? Amene yamukwana nguwo avale
Mwale Enet
9 years ago
Ameneyu ife sitikumudziwa
bobo
9 years ago
zachamba basi
Chokazinga
9 years ago
Williams Gondwa satha kunenelera Chizungu ngakhale programme ya Sports ya Chizungu mutiuze munagwirisa njira zanji posankha anthuwa,koma iwe Tiya ndakudandaula koopsa ndikhalidwe lako unathesesa Sponsorship ya ESCOM chifukwa cha mabodza ako.
To be honest most people listen to his (gondwa) commentry than uyu mukuti khalakaleyo. kodi mukufuna kumakhomerera achinyamatafe bwanji? he deserve it. if not satisfied listen to him next season
Iweukuziti Chokazingawekunenerera mpira mu chichewa sikuti asapambane ayi. Ndiwe MBULI wamva? Botswana,South Africa,Mozambique unamva akunenelera mpira m’chizungu? Ku UK unamva akunenelere mpira mu Chichewa? Ndiwe GULO.
Kodi Gondwau akapose mikoko yogona wayamba liti unenelela mpira ine ata sindidziwa ndipang’ono pomwe ai pafunika kufufuza bwino mungaphe tsogolo lankhalakale chifukwa azichita ulesi
Abale zafika Best Commentator ku Mpira mphoto zakutiko timaziwa ife ndi Best Presenter and Reporter where are these awards are coming from iwe Tiya sitikufunanso ku Mpira
Kumalawi kumeneko chirichonse amapanga katangale zamkutu olo mutapanga kompeya gondwa pasimango sangamake amangokuwa baxi “MWAYI!!!! KOMA PAMBALI PENIPENI PAGOLO”
kodi pambali pamakhala penipeni???? stupid commentator malawi have,,,[GONDWA]
mwasowa chonamizila. Dangerman has got a touch simanngo simango what? Amene yamukwana nguwo avale
Ameneyu ife sitikumudziwa
zachamba basi
Williams Gondwa satha kunenelera Chizungu ngakhale programme ya Sports ya Chizungu mutiuze munagwirisa njira zanji posankha anthuwa,koma iwe Tiya ndakudandaula koopsa ndikhalidwe lako unathesesa Sponsorship ya ESCOM chifukwa cha mabodza ako.
100 percent injustice to the veteran Patrick Simango