Email a copy of 'Cop implicated in K412m Malawi bank robbery' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Cop implicated in K412m Malawi bank robbery' to a friend
Malawi Government intends to arrest two prominent opposition People’s Party (PP) legislators from North, Harry Mkandawire and Mzomera Ngwira, on...
Well it is bound to happen when you under pay ur staff. They have lives to live and families to support. Revise the minimum wage to atleast 20 to 25 grand a month and revise the salaries of civil servants country wide. Amene aziba arrest them and give them stiff purnishments coz they are just thieves bansi.
atumbuka kuba.
WE WONDER, THEIR SALARY IS WORSE IN THE CIVIL SERVICE BUT LIFE STYLE IS EQUIVALENT TO ILLOVO MANAGERS. THEY DONT COMPLAIN OF CRUEL ECONOMIC CONDITIONS MOST CIVIL SERVANTS COMPLAIN OF. KWIBA, UNKHUNGU. 5000000000 MTS AYI BWENZI MUTALEMBA NTCHITO MPHIYO TO BE YOUR BUDGET ASSISTANT
Iwe ukungonena,ngati mukundiva enanu.apolice,aprison anthuwa amagwira ntchito yotamandika koma ka salary 20,000.Abwana ndi awo atinamiza kuti tisiya kulandira change then 24.5% zasiyana pati?musiye wapolice yo akapeza mwai ndi wake iweso ndi mwai wako.
A Police ya ku Malawi kugwira ntchito yoononga mogwirizana ndi akuba. Amalawi anzanga dziwani kuti umbava ulionse wa mfuti, a Polisi amakhala pompo.
KUBA NDALAMA MORE THAN K5Million MLANDU WAKE NCHIMODZIMODZI CASHGATE, MILANDUYO ANGOWAZENGERA LIMODZI NDI AKANGANYA ANZAWO A KU CAPITALHILL. AWA TIMAWATCHULA KUTI ANANKAFUMBWE ADZIKO.
AKATI WAPOLISI WAGWIRA NTCHITO YOTAMANDIKA M’MALAWI MUNO, NDIKUBA BASI
Kodi mainawa ambiriwa akundi mvekera ngati ochokera dela limodzi, mtundu umenewu ofunika kuotcha onse basi!
Iwe azijo ndiwe onama business yanji pa malawi yowina k5o,ooo patsiku. Nanga Ungalowetse capital yochuluka bwanji?
kani mapolice ndimbala zooopsa chonchi