Email a copy of 'Cop Naphiyo knows Njauju killers: Arrested for bragging he knows assailants' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Cop Naphiyo knows Njauju killers: Arrested for bragging he knows assailants' to a friend
Ministry of Health has said K13 billion which donors have pledged to pump into the collapsing public health sector will...
wathuwa wasatipake mpoza mmaso angobwera pa air atiuze kuti talephera chifukwa zomwe akuchita sizikuoneka
Zakumowa chamba eti
Jully nkale koma mukanachitapo kanthu
Surely Naphiyo must have been acting on instructions from “somewhere”. We are waiting…..
DPP WOYEEEEEE
Zamkutu. Zamowa. Anthu kumowa akalezera anganene chirichonse kuphatikizira Ndamwera zanga. Atamwesedwa. Can you then trust kuti wamwera zake?
Play games, keep on fooling Malawians
apolice nonse including the IG zipsyenthe zanu uyu palibe chifukwa chomumangila owo mukuopa kuti akanawulula zambirieti?amamva mabwananu mukukambilana kuti zatheka takonza tinatuma uje ndi uje basi mulekeni muthu wachilungamoyu awulule zambili
This is an issue more to do with ethics than crime. What some people are failing to understand is that pa mowa pamakambidwa nkhani zambiri. It’s not that Naphiyo just came from no where and bragged about knowing the killers. Anangokamba maganizo ake ndimmene akudziwira pa nkhani ya Njaunju yomwe imakambidwa. Now as a man in uniform ethically he was supposed to remain silent regardless of what he knows on the matter. But you know pa mowa mmene zimakhalira. Sometimes you lose your senses and talk too much. The main issue is that he linked the murder to DPP. That’s… Read more »
Intoxication Is Not Defence In The Court Of Law And Naphiyo Knows This.Ngati Mmatamika Kuti Mumwetsedwe Mowa Mwafa Nayo Dala.