Email a copy of 'Court OKs Malawi Savings Bank to sale Mulli assets: Pegged at K3.3 Billion' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

85 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
kapoli
kapoli
8 years ago

ndkazule chnangwa changa ndphke.madzulo ndkabweze k70 ya nima.

pressure
pressure
8 years ago

Kani wolemeranso amakhala ndi ngongole. Ine ndinkangoti ndine ndekha

Ayisova
Ayisova
8 years ago

Mpakana chi MK4.97 BILLION. Onse anangoti kkkkkkkkkk

Kaphulika
Kaphulika
8 years ago

Musiyireni mwana katundu wake. Inuyo mukagulitsa mzanu atsala ndi chani?

Pichi
Pichi
8 years ago

Ndiye kuti ma NGO ndi a opposition amanamiza dziko eti? Amalawi tidzuke athuwa asatisewere juga. Political milage ivuta apa. I hope boma liwafotokozera bwino amalawi and show what the opposition and the NGOs connived to do. Shame on you. Ndisamve wina ku parliament akuchita sabottage budget on MSB issue. Bola ya accountability’yo ndimva koma iyi ayi. Closed story.

Shadrick Gologolo
Shadrick Gologolo
8 years ago

We will never cease to be hoodwinked by governments.I don’t think there’ll be a government that’ll put the welfare of Malawians at heart.The world is full of selfish,progandists and bloody bandits!

Shadrick Gologolo
Shadrick Gologolo
8 years ago

We will never cease to be hoodwinked by governments.I don’t a government that’ll put the welfare of Malawians at heart.The world is full of selfish,progandists and bloody bandits!

bernard
8 years ago

When god says no who can say yes !!!”

Ineyo ndi Ineyo
Ineyo ndi Ineyo
8 years ago

Koma anthu ku skulu munapitadi? Loans are given on collateral, ndekuti Mulli yo kolatero yake inali imeneyiyi kaya. Sangangopita kuka landa Chombe Tea Kapena National Bus opanda chilolezo cha Khothi.. Olo mumunene chotani ndi clever business mani be basi, wangopeleka zinthu zimene sizim’mbweletsera phindu. kungotinso aMalawi nsanje zinakuchulukirani, anakakhala m’mwenye sibwezi mutalankhulapo, Koma chifukwa ndi munthu okuda Basi, mwati mulankhulepo. Munthu olo mumunene, akudyabe his hard earned millions, billionsinso mwina.

Teacher
Teacher
8 years ago

Gulitsani Chombe Tea company, National Bus, ku Chikangawanso uku, ndi iyi imapanga za mankhwalayi, kaya mumati chani kaya, ma tanker ali mbweee awanso gulitsani. ZImenezi ndi zomwe zingagulidwe mwachangu osati mukutsatsa apazi. Zabodza izi zongofuna kuphimba anthu mmaso kuti budget idutse

Read previous post:
Dumbo Lemani’s memorial service Saturday in Zomba-Thondwe

The Lemani family will on Saturday hold a memorial ceremony of the late Reverend Dr. Dumbo Finly Kamwendo Lemani which will take...

Close