Email a copy of 'Court suspends Muluzi case: Malawi ex-president lawyer argues charges were ‘politically motivated’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Court suspends Muluzi case: Malawi ex-president lawyer argues charges were ‘politically motivated’' to a friend
Kondi Msungama, who has officially resigned as Big Bullets FC chairperson, has said he will be more than willing to...
Mulekeni Dr Muluzi kumunzunza pankhani yandale ayi,Muluzi is the best president ever ever Malawi had
u r talking about Muluzi nanga Bingu anaba zingati nanga JB komaso iweyo Peter ukuba zingati. Musayalutse Malawi andale nonse pathako panu
Koma malawiyu..tinabadwiranji ife?
There goes my favourite president.!!!!!!!!!!!!!! mufune musafune, he was the best there ever was.
That is why muluzi akukondana ndi peter in order to gain favours
Lawyer koma ameneyu
Atcheya Woyeeeeee
Kodi anthu andale inu m’matitenga aMalawife ngati zitsiru zanu eti?And now how much of our tax money is Bakili going to get in damage and compensation.And very soon you tell us Atupele is minister of ….cum second vice president.Why fooling the entire Malawi nation on a fake case where yet Malawians are losing out? Uve ndithu.
if you want your sins tobe forgiven, 4giv others first.
Iwe wakutsona khutu ndiwe womvetsa chisoni kwambiri.Bwanji ukutukwana chikhalirenicho watchulanso Yehova.Iweyo ngati sunachite tchimo lina liri lonse ku ntchio.pabanja kapena mmudzi mwako,kweza chala mmwamba.Pamaso pa Mulungu tchimo ndi tchimo.Ndikukumbutse,watukwanatu apa.
Wobera anthu wosauka nonse !!
Lawyer ndi judge wamkulu ndi
Mulungu NAMALENGA
Sangalalani kondwani ndi mahule anuwo
KOMA MUWONA CHIWELUZO CHA MULUNGU PANSI PANO KAPENA KUMWAMBA