Email a copy of 'Criminals steals money at Chikwawa police, escape' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Criminals steals money at Chikwawa police, escape' to a friend
The South African Times newspaper which published an article about Malawi’s former president, Joyce Banda facing arrest in connection to Cashgate scandal...
Inde mbabva zimagwira mbabva zinzake koma apa ndiye tatuma khwangwara.
Chitetezo tinasinthanitsa ndi Ufulu wakuchita chomwe munthu akufuna basi.
Nchifukwa chake ana amasikuanofe sitiiwerenga police, nthawi zambiri timangolanga tokha, cauz dats de only best solution to minimise umbabva.
Mbava zotchedwa apolice ine wina ndizatema ndithu
Agalu inu a police musamanamizira anzanu bwezani ndalamazo ndipo ndinakamba kuti malawi ngati wabvuta ndi umphawi ndi boma lathuli lalemba apolice ambiri akuti kuonjezera chitetezo kuli kuonjezera mbava mkumati a police
DONT JUST SPEAK ON RADIO BUT ACT BEFORE IT IS TOO LATE MR KANYAMA
Police inatha!!kwatsala mbava only!
Does this really make sense to you the law enforcers. This is where and why the general public is losing confidence and trust in you.
Commander in Chief/ I G ,please continue cleaning up the mess in the police.
You will certainly have the support of the general public and corporate world.
kanthu akoooo!
may ALLAH protect our beloved land Malawi. ameen.it hopeless now
SHAAAAAA…CHE KAMYAMA? NDINAKUUZANI SIMUZITHA MBAVA ZANU ZA POLICE…..90% YA ANYAMATA ANU NDIONUNKHA.ANZANU AWALEPHERA KALE.HEHEDEEEE..
This is Police Cashgate. MMalawi muno apolice anapita ndi Dr H Kamuzu Banda. Panopa tangotsala ndi alonda okhaokha oyenera kumayang’anira mma min shop.