Email a copy of 'CSOs accuse Mutharika of attention-diverting tactics on Malawi woes' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

32 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
BigMan
BigMan
8 years ago

Trapence, surely you are the one who is obsessed with anal sex between two men and muff diving between women. You write about it every week in the newspaper, basically your NGO is a full fledged gay club.

TA Khombedza
TA Khombedza
8 years ago

kkkkkk ife mafumu wathutu ndi pulofesa yemweyu. Tonse takonzekera vote yathu mu 2019 ndi ya Pulofeesa Mutharika. Mumvatu m’bebe nangatu ife atilamulira basi kkkkk. Za ugay zanuzo kwanukonko. Ife tifuna wotipulumusayu.. APM yemweyutu basi. Asaaa, anthu osayamika inu.

Alungwana
Alungwana
8 years ago

I think it is stupid to keep on thinking that Malawians can be diverted from talking and discussing the strugles they are going through.

Thikiwa
Thikiwa
8 years ago

Koma ndiye mumva kuwawa mpaka 2050 coz DPP ikulamulirabe mu zaka zonsezi……..

Wilhelm
Wilhelm
8 years ago

They have hit the nail on the head. Sadly, most people seem not to be noticing it. And that’s exactly the point of these tactics. How often do they talk about the economy or even their own economic programs such as housing subsidy? But the moment they mention sexuality, prostitution, abortion or homosexuality the media and public’s interest is inflammable. It’s nothing new of course, it is a well-worn tactic of populists and demagogues all over the world to distract the public with ‘controversial’ issues. Meanwhile, the economy that actually affects the every-day man or woman’s livelihood can be mis-managed… Read more »

kholowa mkabudula
kholowa mkabudula
8 years ago

Azibambo kuikana kumbuyo sikunayambile lero abale,nthawi ya Loti zinali mu fashion mpakana amkafuna kuti apange angelo ndipo mkwiyo wamulungu unakulilakulila pa sodomu ndi gomola. Kuikana kumbuyo ndi choice chawo asiyeni pakuti mulungu kunjakuno alipo ndipo adzaweluza yekha musamukhalile pa mpando ayi. amayi kugwilana maliseche okha okha ndi tchimo chimodzimodzi kuba,miseche,kusowa chikondi ndi tchimo lina lililonse.Ndinu amalawi angati amene muli oyela pamaso pa Yehova? Timamuchimwila mulungu tonse munjila zosiyanasiyana,ndiye tisaweluze amzathu poti naye Yehova ndi mulingo omwewo adzati weluzila. Mwina a fazalawo akanadandaula kuti a Malawi tikuchimwila ambuye tisinthe without specifying then ndikanamva poti palibe tchimo labwinoko pamaso pa a mbuye.… Read more »

Okhrana
Okhrana
8 years ago

Brazilian wax, APM whether dull or not, ufune usafune akulamulira mpaka 2019 then another 5yrs kenako Amfana Chilima naye zake 10, iwe ukudikira a claver and intelligent pulezident, ndiye umvatu kuwawa coz uwl need t wait kkkk

Odi Ukooooo
Odi Ukooooo
8 years ago

What a dull president can speak an individual’s opinion, when he is actually speaking to the general public!

...
...
8 years ago

Zonsezi chifukwa cha Mbendera, anatilakwura galu ameneyu.
Pulofesa wa Cypruss University of texas yu ndi madeya eni eni.
He is a complete loser.

Dorobuchi
8 years ago

Kungoti achina trapence awa ngovuta kuwamvetsa. Iwowo tikamati akugwira ntchito amakhala akunena za mathanyula. Pano nde akuti HE is diverting people’s attention? Akufuna atiuze chani makamaka?

Read previous post:
Witchcraft plane crash’ causes commotion in Kasungu

Kasungu Police Station and Gundani in Kasungu District, on Monday became centres of attraction on Monday as hundreds of people...

Close