Email a copy of 'CSOs call for ‘active citizenry’: Hold Malawi govt accountable' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'CSOs call for ‘active citizenry’: Hold Malawi govt accountable' to a friend
All is well that ends well. And that is exactly how the 2014 football season can be summarized on club...
Amalawi anzanga tiyeni tisayiwale kuti Nkhondo ya ufulu umadzimenyera wekha.Anthu aku Amerika kaya Botswana sangabwere kudzatimenyera nkhonthoyi;palibe.Apo bi tikhala akapolo a atsogoleri wowasankha tokha mdziko lathu lomwe mpaka muyaya.Nchiphinjotu ichi; chifukwa cha mavoti athu womwe.Why?Demokalaseyo ndiye ilipati.Uku ndiye kubetsa poyerayera. Atsamundatu adapita.Lero akutipha,kutizunza,kutibera ndi ana obala tokha(powavotera);Bakili,Bingu,Joyce B pano ndi uyunso nchaka chomwe sanathe…Nacgate…mfundo zakenso sizikuwoneka komwe akulowera.No wonder the economic engineer started very well but was unfortunately misled and changed to become stubbornly unpatriotic,unreligious, undeplomatic etc.And Malawians suffered the worst. So 13 Jan 2015 is the to tell these dictatorial democrats cum ‘political strangers’ that enough is enough! Malawians… Read more »
The economy which your JB squandered is being stabilized now and the Kwacha is gaining strength. As of NAC, what’s K5m as compared to K73m which Joyce Banda foundation abused? Shame on you, people who dwells on chaos of my motherland. Just concentrate on your gays and leave Malawi alone.
This is true if. Malawians want to move forwad we must now rise up and speak against any form of abuse of our resources by the
This is emotion message why guys
MAY GOD THE SAVIOUR SHOWER HIS MERCIES ON MALAWI (THE SO CALLED WARM HEART OF AFRICA ) FOR THE SAKE OF OUR SONS DAUGHTERS AND GRAND CHILDREN (PRAYERS )
Ayi bodza apa palibe uyu mtumbuka or m’Chewa or Ngoni or mYao. A Peter boma lawalaka kuyendetsa. Anthu timaganiza kuti kusintha kwa boma timva zina. Koma kumamvanso za abuse ndalama za NAC ayi zogwetsa ulesi. Much as Tumbukas have some ethnic problems but here I choose to disagree.
Atumbuka amzanga amenewo mwagundika kutokota amai atakuthawani.
Osawanamizapo amalawi apa. Anthu anacenhera amadziwa kuti kumbuyo kwa zocita zanu inuyo mumadyerapo. Nanga mungatiuze komwe mumatenga ndalama zodyera panyumba panu. Komanso kodi munacita declare ma assets anu kwa Tukula?
Mwasowa pogwira pano mwati muwanamize anthu kuti tiyende kumseu kuti ena akupaseni makopara. Shame on u.
Transparency and Accountability will work in Malawi when all the cashgate thieves faces the hangman noose.Forfeit all the property of cashgate thieves and. Return all the money to govt to make it start working.
Atumbuka inu! U cant fool the nation. Malawi is more important than ur tumbuka agenda.
Stupid alesi ma CSO inu. Kukacha ntchito mma lounge a mma hotel kulemba ma proposal a donation basi. Your job is just press releases. Can you also be transparent enough to disclose to us how you get funded and how you utilise the money. Men like you need to have proper occupation.