Email a copy of 'Davido rocks Malawi capital, plants ‘celebrity tree’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Davido rocks Malawi capital, plants ‘celebrity tree’' to a friend
US pop star Madonna and rapper Gucci Mane have raised $5.5 million from ticket sales and live auction to be...
Swag ya mbola ngati imeneyo!
Shaibu, U have spoken sense.Titengerepo phunziro apa.U respected him[Davido}but he did not see U as people.He totally gave U his PRIDE.Even nyimbozo zina zimamveka kuti mulibe malangizo a umunthu.A Malawife UMUNTHU WATHUWU,TISAMAPATSE WINA ALIYENSE NGATI AMENEYO.Mawu amati: ‘RESPECT THOSE WHO ARE RESPECTIVE’.Becoz
they know what it means.Ine ndimauza ana anga kuti; I don’t like his songs,but they urgued,koma sono nawonso amva okha zomwe wachita musician wao.
DAVIDO, WHERE EVER U ARE,’ A GOOD NAME IS BETTER THAN RICHES’
why dd u nt invite Koffi Olomide ? Mumafuna za satanikizo ?ndy tu eeee!wakupangani adopt in a satanic way , nxt tym invite Koffo olomide.
Opusadi ameneyu!!!!!
Useless singer
Za ziiiii. cerebrity ndiye kuti chani
Fu….. Whoever called this idiot. Why are we so happy swimming in mediocrity? Nyero zanu
Hahahahaha people are commenting as if they have grey matter in them but all are empty comments. This campaign has opted to use this FAMOUS star on the international stage than our myopic malawian singers who fail to sing
Manganaye munkhaniyi amafunika kuti atchilidwe? Zopusa basi. Mpaka iphone kuitchula?
Malawi Malawi Malawi my country. Tumatengeka ndi woyimba akunja kuwapatsa ulemu ma newspaper, media, atolankhani kulemba ubwino wa munthuyo even a Police amakhala busy apa ndi apo akuti security but yet ma musician athu eni eni akapita kunja palibe even newspaper imodzi imalengedza. Even oyimba otchuka omwewa palibe especialy in South Africa I had never seen any paper, media, radio station kulengedza za oyimba from Malawi. Koma kwathuko oyimba akabwera akumachita kulandilidwa ndi minster with a government convoy but yet athuwo akabwera kuno even area manager sadziwa kalikonse unless amalawi omwe ali around that side. I did feel so sorry… Read more »