Email a copy of 'Do not be coward on HEQs: Mutharika told to face Malawi MPs grilling' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

47 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mlomwe Ozindikira
Mlomwe Ozindikira
8 years ago

hey a malawi anzanga President akuimirira malawi yonse, monganso ma Mp ayimilira madera mwawo. Chotero iye ngati president ayenera ndithu kukayankha mafunso a ma mp, amene akuyimirira mu malawi amene sangathe kumufunsa mtsogoleri wao. Izinso zili mu mala mulo athu; ndiye mukakhala pano kubakira president chifukwa chifukwa nd wa dpp or mlomwe ndiye sakuyenera kupanga chinthu choyenera, mukungowonetsa umbuli wanu

Wllly Kaslsi
Wllly Kaslsi
8 years ago

Apita nthawi ikakwana
Olembanu talembaniko zamavuto ali mdziko muno osangoti za
ndalezo basi.Olamula ndi olamula basi tidzingokuwaaaaaaa nkumangotuwaaaaa iwo akungonona!!!!!!!!!!!

mulhomwe waku Luchenza
mulhomwe waku Luchenza
8 years ago

Aaaaaaahhhhhh tchulani cholozeka chomwe wachita bwiyanuyu???? One of the worst government we ever had,,,,, ndakutlukani Alohmwe inu

Roots
Roots
8 years ago

Muhome/#41

The issue at hand is not whether APM will answer or fail to answer. We know he is a competent person, all the house is saying, APM should appear personnaly. UR diverting the points and instead you are showing your allegiance. Sizimenezo mdala iwe

Masautso Muhome.
Masautso Muhome.
8 years ago

To those of you who don’t know Peter,you are mistaken. He is never afraid of questions but takes time before he makes a move. He doesn’t even comment on an issue before understanding it fully. He will come to Parliament very soon,but didn’t want to talk neither comment about it. The nation will be shocked on how he answers questions from different topics and angles. Anthu amenewatu mu uwiri wao anabadwa odalitsidwa ndi nzeru. Dzikoli lavuta kulamula one year imeneyi kamba kopanda donor support mu budget,muona anthu nomwenu mukulalatanu mukusintha mawanga muchaka chachiwirichi. Zitukuko akupanga mwachinunu pomwe inu mukuchedwa kumukoka… Read more »

Gule Wamkulu
Gule Wamkulu
8 years ago

Hon Chakwantha, kodi mukwatirana liti ndi Seodi? Musakhaletu mumangokwelana ulele!

dar
dar
8 years ago

Anthu nonse mumve izi; Boma la Peter silamasewera? Zii ameneyu siwabwino wati duuuu sikuti wangokhala ayi; Usiku cha ma 12 midmnight ndi anyamata ake ali busy kutenga Briefcase full of money akulowa mmanyumba mwa wina aleyense amene akuonneka ngati dolo against pa khani ya MSB; Kukhutula chuma kuzunguliritra sitting room ndikumuuza kuti mawa lake asiye kulakhula za MSB or achoke M chipani. Bambo uyu ndikatakwe pa khani ya BRibes and Corruptions: akuti amalawi sachedwa kuiwala 2019 ndi kutali. Okana ndalamazo follow Raphel Tethani masewera palibe. Tsono mukamalakhula mudzidziwa zimenezo komanso Masonic imanena kuti Lawyers,police, Atoney Generals, Presidents shd be members;… Read more »

mulopwana
8 years ago

zitsiru zina zopanda nzeru zikudana ndi nkhani yofunikayi.Appearing b4 Parliament is part of the President’s responsibilities.And yet some low minded pipo say if he is busy he will not go,.The problem with Malawians is ;most are selfish and unknowleagable that’s why when voting they vote in that respect.shame malawi kuba sikungathe choncho.

truevoter
truevoter
8 years ago

nthawi yanu idzafika and ana akumkaka ndamene adzukufunseni mafunso anuyo plant them and you will reap. dyera bwanji atsamunda inu

Peter Mathanyula
Peter Mathanyula
8 years ago

Zidula mtengo ia a pathetic being. Malawi constitution was not written by MCP. If you have personal hatred with MCP that’s your problem. The constitution requires the president to go to parliament to be accountable to the people of MW. And for your your own information there are DPP MPs in parliament who would want to ask Mr Ibu some questions. What type of professor is this who fears to answer questions from MPS. Mbuzi yopanda manu mkamwa.

Read previous post:
North Malawi registers 100 percent increase in sexual assaults – Police

Police in the North say they have registered a 100% increase in the number of defilement cases across the region...

Close