Email a copy of 'DPP fire ‘confusionist’ Silungwe as its Karonga district Director of Youth' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DPP fire ‘confusionist’ Silungwe as its Karonga district Director of Youth' to a friend
National Registration Bureau (NRB) under the Ministry of Home Affairs and Internal Security will from June to December 2017 be...
Kodi ku DPPso amafayana timati ku MCP kokha hahaha! a APM amukhulukire????????
Chenjerani Ku MCP. He may decide to join you. Uyu ndiye ai. China n’china fisi anakana nsatsi. Yekhayu wanyanya.
Kodi a DPP amachotsananso mchipani? Ndimaona ngati ndi a Congress okha. Kkkkkk
Democracy yavuta mchipani cholamula.
Wavisanga Silungwe is a scammer. He is best known for running “Karonga Polytechnic” which is a fake entity. He claims it is approved by Unisa but it is not. He is taking money from prospective students and then delivering nothing. He has over 100 cases running against him in connection with this scam.
Anyani a dpp kusekana zikundu. Koma dziko
Silungwe akanatani pakuti mwana mbuu make mbuu palibepo za chilendo apa. Anyani kusekana zikundu.
KU KARONGA kulibe DPP ndiye anasochera.Business zonse anawalanda ndi chimanga chomwe kuyamba 1tin to 30 tonnes ndiye atayilenji nthawi yokhalira muchipani cholesa anthu mabusiness.Ku karonga anthu azolowera kutakata ndiye iwe uziti nyooooooooooooooooo ndi chipani chosausa chopanda solution ya zovuta .Kagwerani komweko .Tingophera kuti nonse mufwe tibwerele chakale cha Bingu or Bakili
Wabera ambiri ameneyo ayaluka kkkkkkkkkkk karonga poly yatibera kwambiri