Email a copy of 'DPP goes to town on Sidik Mia' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

30 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Bitilinyu
Bitilinyu
8 years ago

Iwe Mwaphelanjiru: Mia sanalemele nthawi ya Bingu, even nthawi ya MCP, baba ache a Mia adali ndi kobili koopsya. Izi zikungooneka kuti Mia simukumudziwa. Ine pano ndikuti Mia ndi bwana sangafanane ndi Kasaila olo pa nkiti. Kasaila adikhilembo 2019 tidzamuonetsa kuti baa Mia akumunyoza leroyu ndi mkadamu.

Mwapheranjiru
Mwapheranjiru
8 years ago

Osadandaula, paja a Peter Mutharika adapeleka Red Card kwa a ndale ongoyenda-yenda muzipani. Izi zathandidza kwambiri a ndale a dyera kumangolowa ndi kutula muzipani. Lero a Nkusaila, a Change Goal, a Zingale Ngoma, ndi ena otero alibe kopita lero, angosala ndi nsaru za chipani cha MCP, UDF, DPP, PiPi, UNIP, ANC, ndi mansanza ena. Tikuthokozeni a Peter Mutharika pobweretsa pfundoyi imene yabweretsa bata muzipani. Zoyenda-yenda ngati anthu amisala zathano. A Mia khalani ndi Red Card yanu, ku chigwa cha Shire. Muzingothokoza kuti Bingu adakulemeletsani nkana mudamuthawa atamwalira kutsatira thumba la ndalama la PiPi. Mudzafa imfa yowawa bambo Mia.

harmonybanda
harmonybanda
8 years ago

which town

Backilie Buluzi
8 years ago

He or she who dumped DPP after the death of Bingu is not a friend in need. I don’t like DPP but that was very bad.

Wantali Savalagogoda
Wantali Savalagogoda
8 years ago

Why not post my comment inu a Nyasa Times kwenikweni iwe Thom Chiumia dyera too much. Post what I wrote as my comment to this story. Ukuopa chani when you copy and paste what Ntata writes? Its not fair what you do Thom. Wadya ndalama iwe and you fear for the truth in other comments- really? Is that what you call democracy? I thought you are supposed to be neutral? Why hide my comment? Since yesterday up to now I keep checking but it is not appearing, why?

Ndeu za pusi
8 years ago

Mia anachenjera osamulora munthu wa dyera amati zalowaso ndale pamene matuluka mu PP akhalebe kunja kwa BOMA mmwenyeyu asaname bodza!!

baggio
baggio
8 years ago

Live mia alone,inu a DPP mukut mia athawa chipani chanu olo mtembo wa malemu usanafike kuchokela Ku South African?mwaiwala inu monsogozebwa mai kaliati munapita pa tvm kukanena Ku bingu alimoyo?NDE mumati mia akhale nawo gulu LA anthu abodzanu maliro amabisa?basi musatikumbutse malemu.mia ndimunthu ozindikila kwambiri or cahsgate anayithawanso safuna zamabodza ndipo ndi munthu wachikondi, wachifundo,okomamtima ndi thandizi.osati enanu olo pankhomo panu anthu anasiya kubwela chifukwa chamoyo wanu akhakha ngat inu

mbuyache
mbuyache
8 years ago

Ochakwera take Mia as running mate, u will not regret

mbuyache
mbuyache
8 years ago

Mia join MCP n show Dpp how strong u r, Kasaila is a nobody in shire valley, u av support also in Eastern region where u av helped alot, centre n north will support u as u a clean guy,akuyamba okha u were mphee, nthawii yakwana show them wat u made of n capable of doing in changing politics in MW, all the best tiri nga nga nga to support this move

Hehehede
Hehehede
8 years ago

Kasa iis not our Lower Shire giant nyonyo takhonda the guy is selfish,rude,arrogant and greedy you can’t compare him with Mia vembe. Kasaila takatata ndi Pitala yemweyo.

Read previous post:
Mzimba mob burns vehicle belonging to alleged goat thieves to ashes

An irate  mob in the northern region district of Mzimba has burned to ashes a Toyota starlet which was allegedly...

Close