Email a copy of 'DPP says MCP’s fears of Speaker impeachment ‘unfounded’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DPP says MCP’s fears of Speaker impeachment ‘unfounded’' to a friend
Police in Chitipa have arrested a 53 old man on suspicion that he stole medical drugs from public hospital worth...
Shaaaaaaaaaaaaaaa clueless impeach the President not the speaker.
Anthu amenewo akusowa zochita, akufuna kuti atitenge ngati ndife opunsa kapena osadzindikira zimene akuchita, tatopa ndi kusowa kwa mankhwala ndi chimanga sakudziwa kuti kuli njala, achoke amenewo.
mcp sidzatheka basi
Ma komenti a Chakwera ndi ankhanza ndikupempha a UDF ndi DPP kuti mugwirane manja sindikufuna tidzaonenso nkhanza za MCP ayi onesetsani kuti utsogoleri usazapitenso pakati anatizunza mokwanira.A Chakwera abwelere ku nkhosa zawo ziwafuna anazibera zija.
DPP mbuzi za anthu osamva kuwauza zinthu akuona ngati ndi ndale iiiiiii malawi ali pamoto
Kumalawi impeachment siingachitike!Since Democracy ndindani adachitidwa impeachment?Mukunamiza ndani andale inu?
Akuthawa mthuzi wao omwe awa. Hallusinations!
You opposition why not impeach the president tikkulira ife kuno kumudzi after all muli okwanira
The name DPP makes me nauseating. I would rather support chipani cha late amunandife Nkumba.
This is the bulshit speaker I ever seen I mean msowoya. We had Louis Chimango and his blood is mcp whatever but he handled issues in parliament professionally the same applies to the late Rodwell munyenyembe (RIP) I will not be surprised once they booted you out, 100% you don’t deserve to lead the parliamentarians in the chamber.