Email a copy of 'DPP supporters in Mangochi celebrate two years of ruling' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

18 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
simbale
7 years ago

Any one has rigths to predict what he or she seing you geofly l swear this is your last term you will believe me,you depend on juju for killing other competrs that is not politics.God is providing us a campable person not like killer.

zomba boys
7 years ago

Kondi uyu wa imvii uyu amati charles jika mulibiretu mutumo olotu olo mmmmmmm chipaningati chikuwonongeka ku eeastern region chifukwa chakulu ameneyu nkhani yake eti,nsombatu basi pena ukakhala mphawi nzeru zako sizigwira ntchito kaya anatengeranji? Ndimamva chisoni mukamati a peter oyeee mukwaononga ndi somba ndakusungira ulemu zambiri sindikamb.

m,baya nikawa
7 years ago

DPP,koma governer wanuyu mumamuziwa bwino bwino kkkkkkk komatu mbuzi zawanthu zikutha mudzimu mudzina la chipani nsalu zachipani akumasithanisa ndi chisebwere koma chipani chinatha simukuona apa pangodzadza ana okha okha kondi angamvote awa nsalire usawatenge a president ngati saziwa ma firm ako ndimunthu wazerutu kwambiri anakuwerenga kale meeting yako kumakhala anthu 7 pena 5 kkkkkkkk watha iweyo kubako usiye kaye

jemus frank
7 years ago

Victoria,ndale simbaliyako ulibe anthu ndi iwe ozikweza wa matama chonyadira ulibenso kumangolanda amuna awathu basi angakumvotere ndani iwe osamazifusa bwanji pakwanu pamene anthu osakumvotera kkkkkkkk watopa ndi uhule uko phuno kuno ndikumati ndikukayamba ndale kuti iwe uzingogulisa mowawo basi chako palibe

APM
APM
7 years ago

This is Mapwevupwevu party, ine ndilibe pulobulemu, amene ali ndi pulobulemu zake zimenezo! Dpp 2019 Bomaaa! Tidzaberanso…zanu izo.

High Time
High Time
7 years ago

Nothing wrong. Kusangalala satumana ndiponso salesana.

Mtelemula
Mtelemula
7 years ago

Victoria Kingstone Hahahahahhahahahahahahahah! Zitheraradi pamenepo

Finyani
Finyani
7 years ago

FEAST OF SONS OF PANGA WELDING DEVILS

Winston Msowoya
Winston Msowoya
7 years ago

Illiteracy indeed,has no defence.These supporters of the party of darkness and indecency are celebrating their own miseries and shortcomings.Since DPP took powers through undemocratic means,nothing progressive economic projects have been laid down to enhance jobs creativity either in the Region or the whole nation.What people have seen of late,is the intensity of corruption,joblessness,violent activities and all the evils,while Muthalika and his closest boot lickers empty government coffers ruthlessly.Anyway,always uninformed masses are the victims of political rogues.

Mbuyache
Mbuyache
7 years ago

Zitsiru. Anthu ena ali ngati agalu. Mukusangalala kuti chani? Umphawi simukuwona, njala simukuyiwona, simunayambe mwabwezedwa kuchipatala kuti kulibe mankhwala, zoti achotsa JCE, PSLCE simukidziwa, zoti chitetezo chalowa pansi simukuwona, ? Ndinu omvetsa chisoni kwambiri. Munabadwa kuchokera kwa anthu koma?

Read previous post:
Malawi coach Mwase’s title hopes in Swaziland suffer blow

Malawian coach Meke Mwase’s title hope in Swaziland was dealt a big blow after his team Mbabane Highlanders were held...

Close