Email a copy of 'DPP-UDF ‘gentleman’s agreement’ broken in by-elections' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DPP-UDF ‘gentleman’s agreement’ broken in by-elections' to a friend
Vocal Malawi leading non-governmental human rights organization Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) has challenged Malawi President Professor Arthur...
simunati a udf akuseweretsani heavy mumasewera ndi ma mafia mbava zenizeni musova
This what we call politics
Achawa sadzadzuka mpaka Yesu adzawapeza ali mtulo tofa nato. Vuto ndikusaphunzira ndiye kuganiza kumakhala koperewera. Dolo ndi Lucius basi ena onse phala lodya baby….a dooooo, kuzolowela kuwedza nsomba.
I was there when this independent candidate presented his nomination papers and he was indeed the man of that day coz he had thousands of supporters who escorted him than any other candidate including that UDF candidate. Koma sindinamuwone atavala DPP t-shirt but black suit mwina mukati za scalf he really waved blue scalf to his supporters koma he has the right to stand as an independent. Inunso a DPP mukangoluza candidate ameneyu ndiye kuti mwatayanso gold ya ndale pa Mangochi chifukwa he seems to be loved my many osati UDF candidate.
We yaos are not mbuli Atupele and his Dadie are. They dont want to relearnt on what bingu did to UDF some time back. Uyisova- mchiyambi chabe.
Kodi nkhani yavutapo ndiyakuyima kwa Wellington Mangulenje? Kodi mmayesa iye wayima as an independent so why is it that UDF seems to be under panic to the extent of calling Atupele to come fight this young lad. Mumayenda mmbali muziziwa ndale za DPP achawa inu mukuwona ngati Professor ndi Chilima ndi opusa eti. Bolani tisamvepo zoti Wellington yu wanyongedwa like Late Kalonga Stambuli paja UDF siyichedwesapo zikafika potelopa. Kaya tiyeni nazoni ife tili phe kuwonera.
Tulo midyomba
If the governance pact is being ignored in only five or less wards what will happen in a national elections? Atupele watch out these dpp guys can not be trusted, don’t tomorrow say say I didn’t warn you when things go wrong.
Zopusa basi
Ndilibe navo ntchitooo!