Email a copy of 'DPP’s Namasasu challenges rerun in Lilongwe City SE' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DPP’s Namasasu challenges rerun in Lilongwe City SE' to a friend
Shop workers in Malawi’s commercial city Blantyre on Monday started a stay away strike that seeks to push their employees...
A Nanasasu, chimene mukuopa ndi chiyani? If you were a genuine winner,people will still vote for you. Unless there is something. Anthu ayamba kukunganizirani Zambiri. Tangokazikitsani mtima pansi.
Rerun ndiye kuti chani, zopusa mudikile 2019 achino cashgate soko inu mxiii
NAMASASU IF YOU HAVE THE MANDATE OF THE PEOPLE THEN ALLOW FOR A RERUN, WHAT ARE YOU HIDING, BY THE WAY THE PEOPLE OF LILONGWE SOTHEAST DONT WANT YOU AT ALL
Namasasu akuopanji? Tivoteso basi ife sitikufuna munthu wina abere. Zobera zatopetsa iyaaaa!
Kodi a Namasasu mukuopa chiani? Ngati anthu amakukondani adzakuvoteraninso. Apo ayi ndiye kuti mukudziwa kuti munaberadi and you don’t see a chance of winning again. Leave MEC to do its work without hindrances this time around.
Y ulibe mantha mulungu amenyabe khondo
Namasasu walephera kutentha court kuti file isowe. Pano wanya, the truth will come out, ndiye kaya ngongole ija mubweza ndi chiani. usovenge.
Ndale za Namasasu zogula mabokosi basi. He bought a Toyota hilux DZ 3660 2nd hand ofcoz when he recieved his parliamentary loan. Beware he is related to Masangwi who was involved in the murder of Robert Chasowa.
I think Namasasu knows that if he looses the next step will be imprisoned as he was involved in the MEC fire. He is a crook as we all know that he is related to Masangwi who murdered Chasowa Robert. Namasasu has that old politiking of buying coffins for the constituents. Talking the millions loan, he bought a Toyota hilux 2nd hand DZ 3660.
Iwe Imran Sadaka zopusa zakozo pa Nyasatimes pano ayi . Uzitiuza za hijab zoona? Chipembedzo cha utsiru, chokupha anthu osalakwa .