Email a copy of 'Dru Hill concert in Malawi cancelled at the eleventh hour: Updated' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

18 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
buke
buke
8 years ago

koma guys kulakwa tu uku. amalawi amationa ngati ndani. bingu muthalika lowerelapo. hiiiiii nnaiwala kuti anafa.

Jj
Jj
8 years ago

Seriously all the way from the USA to come and perform in one of the poorest countries in the universe! How much money did they think they will make?

KCI AND BOBO
8 years ago

Koma KCI and BOBO Part Two munagula ma ticket mwabesa bola mukagula chimanga chotapisa pa admarc kapena nandolo ku united states of mulanje and thyolo

Mphambe
Mphambe
8 years ago

These are washed up perfomers. They are not even remembered in the USA. They probably failled to show up because they couldnt afford their plane tickets. They are on welfare benifits for god’s sake.

Ghadhaffi
8 years ago

Acita bwino kulepher,asatana acabecabe amenewo ndi timphutsinso topanda ulemu timaoneka ngt ntokhupuka tili tiakapunthabuwe tacabecabe,tikagona mmahotel mwathu timanyoza kt ati tagona mzimbudzi zakwawoko,bill ikatuluka mpaka pa K1million timalepheranso kulipira nkumat ndalama yaculuka mapeto ake nkutiphwanyiranso tmakompyuta tathu. Kodi mmesa achina a Joe Gwaladi aliko? Nanunso a airtel(nchira wa mphepo) mmalo mowatukula achina Joe Gwaladi,Piksey ngakhalenso Gides Calamanda inu byz kufuna kutitukwanisira mahotel athu? Athuwatu amayamika ngakhale kuwaudza kt akaimba Bangwe CDSS Hall amanyadira ngati wawaudza kt akaimba ku Oxford University Hall,kkkkkkkkkkkkk mmalawi kutengeka nd zakunja kkkkkkkkkkkk tafanana bolanso ine ndili wa Bandu/Najanji/Shapa/Sakalamento zikundiyendera.

Nyapapi
Nyapapi
8 years ago

Basi ndizamgovaya pa grand ‘n’grill nkavine general kanene

Dwambazi
Dwambazi
8 years ago

Did anyone believe that Dru Hill was coming to Malawi…??????

Paka Bush
Paka Bush
8 years ago

Ife anadziwa kale kuti Dru Hill sabwela alibe fans pa Nyasaland…Airtel kususuka….Bwezani ndalama wama Ticket….

KWACHA DZUKNI
KWACHA DZUKNI
8 years ago

KIKIKIKIKIKIKI KOMA ZINAZI ABALE

Titus scot
Titus scot
8 years ago

Achita bwino angatithere forex, ha ha ha!

Read previous post:
Jappie chides donors, mocks Malawi journalists over Information bill

Information minister Jappie Mhango says government will not be stampeded into passing the Access to Information bill into law under...

Close