Email a copy of 'Dynamos to arrive on March 4: To play Bullets in BT, LL' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

10 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Elias Mwandila
8 years ago

Tayilandila D tichita nayo. Alindichilonda ndiye amvera kuwawa Bullets ilibe plobrem

Anafi
8 years ago

zilibho

Anafi
8 years ago

mulibho maule ndiye kuti ntchito ikugwilika

Lomwe Jackson
Lomwe Jackson
8 years ago

Kkkkk silver ikupezeka boma lanj makape inu timu yamasapota 11 okha basi kkkk

yazula
yazula
8 years ago

comment no 1, ndiwe mbuzi kwambiri & 4 your own information kepe ndiweyo + family ya kwanu,nkhani ili apapa its about Nyasa Big Bullets vs Dynamos did they talk about Silver Strikers here? inakakhala kuti Silver yakoyo imatha mpira si bwezi ma player anu atathera ku Mozambique ayi, leave us alone(NBB) ufune usafune NBB ndi peoples team basi & pa MW pano ndife no 1.

stephen
stephen
8 years ago

mwaitha. ena awonera

innocent gama
innocent gama
8 years ago

IS KELVIN MOYO gs OR VICE gs ?where is the GS ? UYUTU NDI WANOMA PAJATU . WATENGA BUSINESS YA DEALERSHIP YA BULLETS PANO AKUMATENGA NDALAMA KU TNM NDI MKAZI WAKE .

A Bullets munthuyu akulemelerani mukuona analibe chilichonse anasala makutu okha lero wayamba kusamba. nyumba ngati amalipililidwa ndi apaongozi.

kangoma
kangoma
8 years ago

BRAVO BB EX. ,TIMAKUFILANI HEAVY

kangoma
kangoma
8 years ago

Expedite the signing of Lanjesi and zoya , otherwise BB u are good in decision making . tikukufilani mabulaz!

mzungumbuli
mzungumbuli
8 years ago

Team yabwino ku Malawi kuno ndi Silver Strickers,The Bankers, Umodzi-umodzi, Mpunga-Mpunga ngati wa kwa govala, Ena amangoti Team ya mabwana. Osati makape awa ozolowera kugenda ma shop a eni ake.

Read previous post:
Msungama free on bail: Drop sedition charges, activists urge Malawi govt

Malawi Congress Party (MCP) supporters on Monday erupted into songs and dances as Police granted  bail  to their member Ulemu Msungama...

Close