Email a copy of 'Embarrassing: DRC boxer knocksout Malawi’s Masamba in round one' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Embarrassing: DRC boxer knocksout Malawi’s Masamba in round one' to a friend
Main opposition, the Malawi Congress Party (MCP) has told the government off on its threat to dissolve Lilongwe District Council...
kupewa kuposa kuchiza osaziyamba dala muzafa ulele.kukhala ineyo ndikadalengeza mpompo basi kuti magolovu ndalekana nawo,ndazitaya bola ndizikabelekera atsikana ana munzindamu.osati anditchole sagwada ulele.
Kkkkkkkk amalawi mwandipangila tsiku labwino.if u want to do well in boxing just cross the bolder as zimbabwians and congolis hav done,com and train in zambia u will do well ndinu abale inu timakunyadilani,hope muli bo?
amalawi tili kutali ndichilichonse,tiyeni tizingopanga mdulidwewu basi
vuto lomapita mu ring ,phonda, maungu zitazaza mimba limenero……ka mimba nguuu katasenza 20kg ya phonda how do u expect to withstand body shorts….u r lucky sunazibibile koma chipwisi unachipulumusa coz nachimvaaaa
Dzina la malowa ndilotemberela zochitika kwa a malawi, tilisinthe, a malawi omwe akulipira/ adzilipira/adzalipira ngongole yomangira malowa akhale ndi mphamvu zopereka dzina lache.
Ndi udindo wa president kubweresa chitukuko mdziko so no neep to clap hands munthu akagwira ntchito yake yolembedwa more over akatisiyira ngongole yoti iye ndi 1 tambala yomwe sanalipe.
Mufuna mudzingochita manyazi chonchi?
Chomwe timatha a Malawi ndi ufiti, Nsanje ndi kuswana ngati ma Jon white
Number 1, You have no base to despise Nsima. Nsima is nutritious. It is a carbohydrate just like rice or potatoes. The issue is what goes with nsima that makes an issue. Western meals start planning their meals with a protein (meat). Here we start our menu with nsima as the main course and ndiwo as the subordinate. That’s where we get it wrong. Now, go back to class with your useless and fallacy innuendos. Anyway, back to the real issue. A Limbani Masamba musazipope. Munaledzera ndi zibakera 7 zokha. Seriously, that boy would have knocked you Dead. Osapanga makani… Read more »
the nsima we eat has most of its nutrients removed. the nutrients are in the “DEYA” how many people eat Mgayiwa? So up to a point No.1 has a point.
Malawi as a nation shall not perform well in any sporting discipline as long as we have nsima as our main diet. Nsima has no nutrients and as a result makes people retarded in everything i.e growth, school, sports, even in bedroom matters. Stop eating the useless nsima and you will start winning in sports, you will also become intelligent in school, we will start having tall and healthy children not the stunted ones we see nowadays and your bedroom performance will improve tremendously.