Even those players nde chambatu you mean someone with his wisdom in the upstairs can leave Zimbabwe or Botswana to look for teams in Malawi. Is that player good or just from the social teams. What are you going to offer a player from foreign country. Ask Be backwords Wonderers aboiut that player from Cameroon.
Kanyimbi
8 years ago
Koma kanthu ndi khama nyerere inakokera bwampini ku una ndithu. Komanso matama ena akufanana ndi a chule olumpha popanda dzenje.
A chatsalira Epac si size yanu takhalani ku silver basi, amenewa ndio ma size kaya mwamva
lets wait and see but be careful coz nthawi yoononga kapena kukonza timu ndi imeneyi.
jst wait n siii mvula ikagwa kuchuluka zolira