Email a copy of 'Escom vehicle kills three, two others sustain injuries' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Escom vehicle kills three, two others sustain injuries' to a friend
Chilumba Barracks FC says they are keen to spend more to bolster ranks in their squad ahead of the upcoming...
Whom 2 be blamed? Pedestrian o drivers,my ans is, drivers coz they over when they reach M1s road 4geting that pple are still there, may there souls RIP
Drivers Please,, Mukuyenera Kuchepetsa Speed,, Onani Mukupha Anthu Omwe Patsogolo Akanathandiza Dziko Lathu La Malawi. Mukamayenda M’misewu Mumakhala Ngati simunayambe mwayendapo pansi. Ifenso oyenda pansi tiyen tisatile malamulo apa msewu, remember to keep right!
Atonga nanu mumakonda kugona mumsewu ,ngati mwatopa kagoneni kunyumba please!. May their soul RIP.
Tresure sibwino ancle kuyakhula moteromo
Please note that most Pedestrians dont fear a vehicle but Rain. Kudelera amati Iri Ndi buleki iyima.
I have been a victim of such Behaviours moti mpaka ena anandiuza kuti ndikazagunda munthu azandiotchera Galimoto, Imagine Such Impudence.
Wakula ndi Umbuli anthu pa Malawi
Kodi ya mwanayi ndiye yamveka nanga ya ku Nchalo bwana District Engineer kupha mnyamata wogwira naye ntchito ndikuvulaza wina a Police anangoipondereza ija bwa. Chilungamo chiziyenda ngati madzi.
Why wasn’t the driver murdered as I read usually happens?
naye angophedwa bas sizomatichedwasazo
Big companies like Escom should make sure to recruit drivers with defensive driving certificates, osamalembelana podziwana ayi.
Please drivers no matter what let’s reduce speed when approaching busy trading centres along the road. Let me take advantage to humbly remind pedestrians NOT the ones killed here because they were walking for a purpose but others I sometimes see idly sitting at the shoulders of the road to avoid that.
RIP