Email a copy of 'Ex-Bullets’ Zakazaka says ‘all is not lost’ after massacre in Sudan' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ex-Bullets’ Zakazaka says ‘all is not lost’ after massacre in Sudan' to a friend
Minister of Transport and Public Works Francis Kasaila has defended the bogus vehicle maintenance of unserviceable and uneconomic vehicles by...
Ife anoma tikuti all is not lost, me these guys shall be beaten again at home. Aganyu tidzamwa wamkaka. Kungotionongera ndalama zathu sms campagn. Mwatilira kuti nyooooo. Chakwanu leka muchotsedwa chimbenene. Akubwera ndi 2 goals pamodzi 6-0. Manoma pa stand yowo ija kumva kukoma. Bullets yatiyipitsira mbiri amalawi.
Ajimy Chipongwe Chimenecho?Mako Ndi Mako Ngakhale Achepemwendo.
Mpira siophweka ………………………..
Wasted baleyu
Aaa onena anene koma ife patsogolo ndi bullets.bullets woye.
koma bullets
All the best maule
Ife a Nyerere tinawapepesa kale anzathuwa ndi K200,000.. ananfedwa nonse. Tikulilananu.
Kaya zako izo ndijelasi yakoyo bola dzina la maule liliko kucaf
It doughtful to have tangible results with that big strong opponent in replay match