Email a copy of 'Ex JB security officer seen as Mphwiyo’s body guard' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ex JB security officer seen as Mphwiyo’s body guard' to a friend
Mchinji district is in the headlines again. Barely a week After an 18 years old girl was beaten with hot...
A mphawi kunyozana apa Eni ake akudziwana, akumadya limodzi ma dinner ku Blue Ginger area 10
Mphangazira anali nyamata wothamangathamanga ku DPP and he is a civilian. Unless if you tell me that he is providing security to the Cash Gate suspect privately. When JB become President he was trained how to handle a rifle and he was one of the trusted guards for JB. Ndi munthu wamba ameneyu olo ku school sanapite. Ngati anafika form 2 ndakayika. Kikikikikikikiki!
mulungu akuona.mizimu yaamphawi ikufuula.pano mukuti tidzilipira kuchpatala.chonsecho ndrama mwabaiba.
ambuye adzaweludza yekha.zibani misonkho ya amphawife.mudzigula ma bimma magalimoto onga ngati achoka pansipanyanja.
kumalawi kuno ndalama ndiomwe zimalankhul, tiyenazoni ine chuma changa chiri kumwamba ndikalankhula kumeneko, afunseni omwe adapita kalewo akakuuzani
Izi akanakhala kut ndi munthu okuba mbuzi kapena nkhuku atamangidwa kale koma ma billion ndizinthu zovuta.
Next time tizamva kuti Mphwiyo anadumpha ku body ya land rover ali mu unyolo and he has smashed his cashgate brain at the Tarmac road.Ndi mmene imathera milandu imeneyi ikafika potentha.Koma anthu timalangidwa pa dziko lapansi mpopano.Mzimu ya anthu imasowa panadol ku central pano ikufuula while others were splashing looted tax payers on beers and bitches surrounded by vultures around pampering him that he is big man.Some was spent in Zuma land on Chardonnay washing their throats with expensive meals while an average Malawian cannot even afford a loaf of bread.Evil people they should all rot in prison and their… Read more »
no one iz above the law,aliyense amene walakwila lamulo aweluzidwa basi
I hope they don’t eliminate Mphwiyo and try to blame on each other including JB. Who assigned this man to Mphwiyo, is it JB or DPP deliberately doing it to raise more suspicions? Is this bodyguard still a government employee or private? Either way it is not an intelligent move by either side!!!
Apa nkhani nzakuba basi,chifukwa chinayambitsa zonsezo ncha??