Email a copy of 'Ex Karonga-ADD boss named prime suspect in tractor scandal, on the run' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ex Karonga-ADD boss named prime suspect in tractor scandal, on the run' to a friend
Chikwawa United owner Owen Chomanika failed to win the hearts of Football Association of Malawi (FAM) affiliates for nomination after...
PHilip am stupid zoona but pm oz in LL attending meettng n palibe wa police adawafunako pankhani iyi n PM nkhaniyi adaimvera panyasa pompa.shame to nyasa repoters.osama falitsa nkhani zabodza.n EX PM is not MR PHEWA afufuze bwino.EX PM is mr yona shupit.EX PM amagwirabe ntchto?mbuli zawathu
Say it’s not true and shame the Devil by proving it.
No doubt that zaya kunkhongo! U must be very stupid with your useless nkhongo. Even a blind could sense something here. If he is innocent and did NOT sell the Tractor,why is he on the run and NOT answering his fone? Why don,t he go to KRADD and tell his side of the story? Bottlomline! He sold the Tractor.
The problem Phewa is not from north. It ve bn oky if it was bought by a northener. It looks auction was in whole Mw and i believe everywhere things happened same way
Zimamveka kuti ku Ntcheu anthu agula galimoto k150 000. Ma yamaha k30 000 pa auction. Auction was in the nation ? Akadagula mtumbuka sizikadavuta
Is It Malice Or Reality? Karonga, Tell Us Realities B4 We Judge Wrongly Or Rightly. Mukuti Zatani Kodi?
Chilungamo chake ndichoti Malawi yafika poola.Kwakhala tsopano tidzava kuti dziko la Malawi agulitsa magamba .Guys chikupangika ndi chiani makamaka? Ndava kuti magamba ena akutsatsa RBM
Wellington Mphewa ndi mchewa wa ku Lilongwe ku Kasiya,wamwa mowa pa KR Salima pamodzi kanyenya wa nkhumba.
you dont know wat you are talking about.mr phewa sadagulitse thalakita ine ndi wa karonga ADD tractor agulitra okha n anthu opanga auction wa adayambira kuchitipa thn karonga n kukaronga adapita ku EDUCATION ,DC’s offces n PVHO becareful ndzomwe mukunyozazo ax ife akaronga ADD nt ktinyozera PM.mowa or atamwa skul mudamuphunzitsa ndnu ?
mumfinye phwala abwenze tractor ameneyu ndipo komwe wagulitsa kwa mlimi ku TZ ndikukuziwa ine mbuzi imeneyi ili mu katoto