Email a copy of 'Ex Malawi High Commissioner Bandawe passed on' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ex Malawi High Commissioner Bandawe passed on' to a friend
Top heavyweights in Malawi music industry have been lined up to headline live music performances at the inaugural event of...
VERY SAD.
MAY YOUR SOUL REST IN ETERNAL PEACE
My home boy, may he rest in peace and we will miss you baba, tate.
MHSRIEP!
koma akafa munthu opanda dzina -profile koma biography yake nthawi yomweyo kuti iiiiiii abale history yoseyi mwaitenga kuti ndipo nthawi yanji.koma akapezeka munthu wa malisece nde zoose ndi ma age ake andi ose a mbanjamo kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
tadhindani cipikicha cao taone
I agree with BlackImage.
Akafa munthu odziwika at least mudziyesetsako kutipatsa ka biography kake pang’ono,,, anabadwa liti? Kubanja landani? School zanji zomwe waphunzira? Wasiya ana angati? Wapangapo zotani? Amadwala chani? Etc . osamalemba ngati mukuthamanga kumapanganso edit musadatsindikize
eti eti amwene mpaka “My Your Soul…….” kaya amathamangira kuti anthu amenewa….aaaaa. Akufunikadi azidekha.
The story is just simply getting information that was made available on someone’s Facebook page. This is just a starter more details will come later. I can’t fault the writer or the editor this is good peace for immediate release. The other details will come during burial ceremony. Bravo Mana for report.