Email a copy of 'Ex ministers Lipenga, Kandodo join Times Media: Tukula fired at Times TV' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Ex ministers Lipenga, Kandodo join Times Media: Tukula fired at Times TV' to a friend
When the ruling DPP is done away with their new-found obsession with MCP president Lazarus Chakwera, the least they can...
Ken Kandodo wachita bwino, that’s a good move, Ndale zake kuKasungu zinatha! The MP there is well organised and sapupuluma, money or no money sangamusunthe! Matama aKandodo ngati kuti timadya kunyumba kwake, Anadya ndalama za stadium ya Kasungu ameneyu, voti akampatsa ndi nda,? Kapena akaime kwatate wake Ku Zomba, komanso kugwilira tiana mkulu uyu, Maya amamvapo chain?
Ayi Tiziona.Kozani Ma Programme Abwino.Tikufuna Tidzionera Mipira Ya Kuno Ku Malawi Ndi Ya Kunja(super League Ndi Barclays).
iwe Usalimbane ndi Pilirani.Iye ndi dolo osati zimabi za demotionzi
Duncan mlanjira kupepera too much. Umakhalira kupempha anthu mowa pochita cover golf and mpira lero uli mmadzi.Komanso upie ku sukulu how can you a sports repoter in malawi for 15 years and above.You better fin else to do.No wonder you still lead a miserable life.Umatenga abale ako kumapita ku engalane ngati akukasewera ma game a olympics ndiye amasala komweko.Ife aku Blantyre print tikudziwa bwino lomwe timangopenya.
Zikukhala bwanji
eh eh eh, anzathu, olo ulovawo mpaka pamenepo? from minister to ,,,,, ayi, chitani manyazi.
Pilirani Kachinziri is not a TV presenter. achoke nsanga, kumango bwebweta nsete program yonse!
Times means ! Nthawi
Congratulations bwana Lipenga and Ken Kandodo. Please do not go back to politics. There is life after politics. Join Ntaba and you will still find food just like all of us do.
Those who have been fired are from which region? Find out!!!