Email a copy of 'Exposed: KB kept vigil at Civo ahead of knock-out tie' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

11 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
knowells
8 years ago

Ma allowance akamasowa timatelo.Nsilikali wanzelu amapanga create ntchito kuti ana apeze kanganyase.inu mmati atani.mzanu mmene yavutila ya Malawimu.

Nyenyezi
Nyenyezi
8 years ago

Kikikikkiki kodi mateam okhulupirira nyanga alipobe ku malawi kuno? ndiye munapindulanji? anzanu a noma ndiawo akuvutika kupereka MK250,000.00 kwa mai a ku balaka nkana analuza pa home ndi CIVO, mpake asilikali anazolowera molingana ndi ntchito yawo, koma zantchito ndi mpira ngosiyana, inunso pantchito simunafikepo, kukabwera nkhondo kumalawi kuno ndipomwe titazaziwe kuti mankhwala anu amagwira apo bii! muzingonyika. anzanu a Jesus as juju ali pa top with 35 points unbeaten pompo dii kikikikikikiki

True Son
True Son
8 years ago

If juju works in football Mozambique could hv bn winning Afcon

mduduzi nyanda
mduduzi nyanda
8 years ago

kuzolowela ntchito zolonderalonderazi basi, zausilu!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

Souja
8 years ago

Musanamizane khini ilipo!!

nobel
nobel
8 years ago

So KB still believes in juju? It’s true that their moving away from Dedza had a traditional belief that Dedza Young Soccer uses juju? I think it’s a sign that they themselves use khini kkkkkk

sandra
sandra
8 years ago

Hahaha if Juju works then Malawi could’ve qualified for World Cup, won World Cup a couple of times, we should have a World player of the year- in other words what Pofera has said is true

Bayangwe
Bayangwe
8 years ago

Anapindulanji?

i miss kamuzu
i miss kamuzu
8 years ago

ngati anthu otiteteza amene akukhulupilila zinthu zopusa ngati za ufiti, dziko lathu lingatsogole? as i’ve said before, mfiti ikadzalenga mankhwala a AIDS or cancer, kapena ikadzatiwinitsa world cup or even africa cup of nations then i will believe. otherwise, it’s all stupid bush business to me. nyo!

Christian
Christian
8 years ago

kkkkkkkkkkiest koma ziliko

Read previous post:
Mulhakho wa Alhomwe to host fundraising dinner and dance Friday: Mutharika guest of honour

Tribal grouping, Mulhakho wa Alhomwe (MWA), which has step up preparations for its annual celebrations in October, will this Friday, September...

Close