Email a copy of 'Fake resignation letter about Malawi Veep Chilima goes Viral' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

25 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Rozwell Mkandawire
Rozwell Mkandawire
7 years ago

koma ngati nkhaniyi ili yaboza chabwino koma ngati ili yoona ndiye tikhumudwa ambiri because Chirima is an asset not only to DPP but also to Malawi as a nation. Ndikuuzeni kuti kudera LA kwathu anthu tinkafuna kuvotera chipani china koma pamene a Chirima anabwera pa campaign yao yongodusa just a few days before elections anthu tinasintha maganizo athu ndikuvotera DPP. Tinaona chinachake mwa iwowo ndiye musatiyese.

Ebuka
7 years ago

Kalata iyi alemba ndia DPP ndi gulu la CHAPONDA ILI INU LIMADANA NDI CHILIMA

solomon
7 years ago

chilima z good n reasoning,calm and clever.that mach i kno

BIMA
BIMA
7 years ago

Chilima you stole our
Votes with these mafias

You betrayed the whole country full time

Now the malawi population
Is suffering cos of you and your Dpp gurus

The guilty feeling is haunting you day and NIGHT I could notice it on
The way of the CROSS

COME OUT OF THE SINKING /STINKING SHIP
REPENT AND FOLLOW
CHRIST MY BROTHER !

THE NATION WILL REMEMBER YOU !

show banda
7 years ago

DPP ZOONA CHIPANI MA POTHOLES OKHA OKHA KOMA MUWACHITA RE SEAL MAENJE AMENEWA. PANOPA SINDIKUONA
SINDIKUONA POLITICIAN WONKHWIMA MAGANIZO,KAPENA MAI JEAN KALILANI KOMA NDI A CENTRAL AMEMNEWO
KU THYOLO,MULANJE MULIBE ONSE MADEYA. APA NDIYE TSAZIKANI MUYAMBE KUMANGA. BWANA CHILIMA
SIYANI YOU STILL FRESH AND THERE IS ALWAYS NEXT TIME. NDIPO MUKANGO CHOKA BWANA CHILIMA BASI
CHIPANI AKUTSEKA NGATI CHIPATALA COPANDA MANKHWALA………..VEEP,VEEP VEEP CHONDE ASIYILENI NYANSI ZAWOWI

kings
kings
7 years ago

Nabanda, ndiwe munthu oyiwala msanga, Muluzi did not end well with his vice president Justine Malewezi, came the big Kahuna he did not end well with both Chilumpha and JB. Even JB did not end well with her vice. So what can stop Mr Ibu falling out with his vice???? Tell us.

Thandie Majiga
Thandie Majiga
7 years ago

How many pages does this letter have. From this page I don’t see any paragraph mentioning about FAILURE TO FULFILL DEVELOPMENTAL AGENDAS, as you, Nyasatimes, are putting it. Please don’t exegarate..

truebut
truebut
7 years ago

Musiyeni Chilima amalize bwino. Anakulakwilani chiyani?

wika
wika
7 years ago

Kodi ena mukuwachita propse wa mufuna akazalowa azizagawa ma condom ndi ma mabanjo mmsakulu eti? M a commedian ndi oyimba ambiri ndi anthu osokonekera mitu. Amanena zina uku akupanga zina. Ndi mmene amapezera mchere wawo koma sizitanthauza kuti kuwapatsa udindo wa u president angawukwanitse..ataaa

Uncle Mugabe
7 years ago

i love my Mother Malawi…..

Read previous post:
Malawi post code and physical address project proving to be a success- MACRA

Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) says the physical addressing and post code project which it rolled out in December 2016,...

Close