Email a copy of 'FAM clarifies on Carlsberg Cup semi-final venues' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'FAM clarifies on Carlsberg Cup semi-final venues' to a friend
Joe Thomas Nyirongo, a Mzuzu-based boxer trading under the banner Aunt Tina Boxing Promotions, has said Malawi has a lot...
ngat asakufuna akhale…..akuiopa noma! !!!
mbali zonse za dziko la malawi zikawonere mpira umenewu basi. malo a bwino ndi civo basi.
Inde wosauka alibe mau ndi zoona, koma if justice be said, Moyale has a case. Why should they play all their cup games away from home? Who made those retrogressive rules? Come rain come sunshine the game must be played at Mzuzu Stadium because simple logic demands it. After all moral rules of the game also require that Moyale’s supporters need to see their team play at home.
Munya muona chakachino. Nomads tengani chikho basi tidzipitanacho ku Lali Lubani Rd, enawa akuchedwa ndi kulankhula…kkkkkk. Abanenelera.
High capacity is equal to higher revenue. Masoja a Moyale can play any team anywhere ndimasoja amadya Beef.Paøibe vuto apa and sponsor on the marketing side akuona ma venue akumadera amene ali ndi anthu ambiri owusisa wamame
let the rules rule the game nt ur kampwathi rider’s thougths! red army on parade.
Noma imayenera kuti ipite ku mzuzu koma osaiwala paja amabelekedwa ndi Walter
how can FAM choose small grounds? money is the ans, stay put it will never be. BT N LL WOYEE!
noma n bb WOYEE!
Ingotengani chikho mupeleke Ku bullets or wanderers ife a moyale sitipita Ku lilongwe, iwe zakazaka ndi fam pamodzi ndi sponsor wakoyo macheeeeende anu
Mitu ya John Chilembwe tiyichulukise Ku bank basi.
We are the only team to carry the cup,moto buuuu!Wina alira,ngati sapita wamoyo.(ST).