Email a copy of 'FAM sends Bullets champions league application to CAF' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'FAM sends Bullets champions league application to CAF' to a friend
Times Group Head of Business News Thom Khanje has donated K50,000 (about $100)towards the Friends of Limbani, an initiative aimed...
God bless Malawi!!!
God bless Bullets!!!
It can’t get better than this!!!
Chitimu cha fuko. BB 4 ever!
Woza woooza BB afuno abwino, komanso ku caf
Good Luck BB to have your application considered favourably by CAF. Should that happen, you need to polish up your finishing and also create a bit more chances. Polish up your finishing from open play and dead balls (corners, free kicks and penalties) because life will be much harder out there. You are not to be the whipping boys in the competition. Meanwhile, a great many congratulations for beating Moyale to be crowned the undisputed Super League Champions for 2013/14 season.
Amene zikumupweteka akakolope nyanja basi!Maule omwewo kuti wawawawa!!!!
kungofuna kulembetsa kuti munali ku caf zikukanikani kuno kumeneko mukapangako chiyani? muchitike mwayi chifukwa cha pasamvute .mwanya
Moyo oyipa monga ine Mmalawi weni weni ku Capetown ndili okonzeka kuponyapo kangachepe kuti timu yofukoyi kuti ikapikisane nawo Zabwino zonse pajatu timati mauletsi mkumadzulo ndiye palibe cholets congraaaaaa my heart team
Pamene enafe timati wathu ndi wa mpungampunga koma kulowa mu CAF C L timaopa.Nchifukwa Chake timangoyankhula kuti tilowa.bravo maulle chifukwa simulowa mu CAF ngati timatimu tinati.
Big team pa Nyasaland,tapangani account tiperekeko kangachepe ife,team ya fuko,all the best BB.
hop u wl do better in caf ,as it waz sometimes back .indeed u r the best kukankha chikopa ndi cholinga .BB take us acros the boarders .mumatha!!!!!