Email a copy of 'Fan regains consciousness as Red Lions charged of misconduct: Malawi Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Fan regains consciousness as Red Lions charged of misconduct: Malawi Super League' to a friend
Murray William KanyamaChiume was by no means a political midget. He was a true African nationalist leader who not onlyassisted...
AMALAWI,,,u dont appreciate kuti dziko lanu mulibe nkhondo coz u’ve soldiers who know how to fight..
taonani even pa DRC pompa the SA SOLDIERS were killed and wounded in the process 2getha with the tanzanianians,,mumafuna abale anu atafa ait????
no matter wat MALAIYA MUSAGENE
Mwawacita bwino kuwaphika mafanao
Sulom ichitepo kathu apa
Search me These brutal army players and soldiers need to have their own MDF league. So far they have several team enough for their own league. We ALAIYA can not play football with these monsters. This is not the first time these hynic styled team of the so called RED LIONS has been to it. Enough is enough, they should not spoil our game. Azisewera mpira ndi anzawo a Mozambiquian Army
3rd Class Shorts FADAMULA’s.You can’t even shoot straight.
Mudzayetsere kupanga zimenezo ndi Bullets, tidzakusosolani.
Bola G4S timayiwona mumageti ndi mabank working osati these terrorists masquarading as MDF. pamusundu pino mose a MDF na sekenemba zinu zambula kupipa
Masapota omwe anagenda bus ya Red lions muwatani? The Referee was clearly biased mumutani? Come out clearly on this one please!
Pamene padutsa uniform yofira ndi choncho basi
Ena mwa asilikali ndaphunzira nawo sukulu. Ndikawakutumura amathawa ndewu, lero chifukwa choti ali mu uniform ati iyeyo ndi dolo. Ndikazakupeza uli wekha ndizakuthyola, ma zulu atizunze iwenso ka soldier olo nkhondo siunamenyepo utivute? Mapazi anu nonse asilikali pamodzi ndi comander in cheif wanu.