Father arrested for having sex with own daughters, breaking virginity

Malawi Police in Enukwenu, Mzuzu have arrested a 43-year-old man accused of having unlawful sex with his own daughters and breaking the virginity.

The man who Nyasa Times cannot name to shield the identity of his children, has been having intercouse his two biological daughters aged 16 and 14 since 2014.

”The suspect is married and blessed with 7 children,” National police publicist, Rhoda Manjolo told Nyasa Times.

Manjolo said the man was arrested on Wednesday after the victims revealed the issue to neighbours.

”On this day (1st April) he defiled them again; and the victims decided to report it to neighbours who later alerted the police.”

He has been charged with incest under Section 157 (1) of the Penal Code.

The sex offender hails from Yolamu village T/A Ntwalo in Mzimba.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Please share this Article if you like Email This Post Email This Post

More From Nyasatimes

More From the World

200 thoughts on “Father arrested for having sex with own daughters, breaking virginity”

 1. Chluwe says:

  Mwatani kodi a zibambo?tamakhalani amanyazi pochita zinthu,mphanvu zanu dzikusintha pang’onopang’ono:-(tapotananu

 2. kholowa mkabudula says:

  Amalawa mchele mdalayu, kungoti anayamba tisanapsye tindioti. Akanadikila tifike 30 mkulawa bwino mchele….koma abale tuwasungwana tikangokongola kuposa amai awo basi tili pamavuto? ufiti umeneu,basi ndasintha maganizo mfuleni ameneyo moto wachulukitsa awononga tiwana!

 3. Boogle says:

  Ndimbalame……

 4. MAMINA says:

  KUFUNA CHUMA

  CHUMA CHA WANTHU AMBIRIWATU NCHAMANKHWALA

  AZIMAYI AKUPILIRA MMANYUMBAMU

  KULANDIRA ZINJOKA ZOMWA MAGAZI
  KUMALISECHE !!

 5. nazimbiri says:

  zosadabwitsa,atumbuka ndi chikhalidwe chawo.manyazi anatopatsa galu oyenda maliseche.
  ena tatoyandikana nawo,koma zimachitika kumeneko zochitisa manyazi abale.mayi kukwatiwa,kuyamba kubereka ana,mkazi pakhomo kumalera ana amn’gono wache,mwamuna m’modzi.

  kupempha mkosayamba,umphawi osanena,kubwereka zinthu mpaka,kwa manebo opanda azimayi abale.atotichosesa ncthito agalu amenewa.mabodza simungatofuna,akakhala kuti atofuna chakudya pakhomo pa munthu

 6. Eeeeeeish???? says:

  Chili ngati chinkhuku chokumwa mazira ake.

 7. Chicco sindathole says:

  Uhawi pera chidoda no zeru

 8. Lilaka Nena says:

  chonchi Ambuye angatipatse mvula yabwino???? machimo ali thoooo

 9. Chibankhuni says:

  Very sory!deal with please!he is not afather why couldn’t him look for prostitute/sex worker if he knws that he is adog,may be a hen,teache him.

 10. kazondo Boyz, NB says:

  Those the people deserves a good penalty. A real man can’t defile the very own his daughter cookies. Is there no whores at the area to relief himself if he is like goat.

 11. pumbwa says:

  nyere yafikanazo pauchitsiru.

 12. Willy Maliro says:

  Signs of last days

 13. Joseph Chikoma says:

  Nyasi zimenezi zikuchulukirabe! Koma nzomvetsa chisoni

 14. Mkonda Amalawi says:

  The fact that he is in Mzuzu does not mean he is Tumbuka.Mzuzu has people from different places.So what is the fuss about Tumbukas when the identity of the person has not been disclosed?

 15. cydreck says:

  Nyere afikanazo pauchitsiru.

 16. Jenifa says:

  Mtumbuka sadzatheka basi! Kukwatana anachita kuchekela.

 17. nankhoni says:

  That man is a wizard…. kumwa mazira ake omwe? Wat a Shame

 18. zoona says:

  kukhwima basi typical of anthu achilomwe makamaka alomwe okhulupilira zaufiti ndi zakumidima. Munthuyu ndi mlomwe kungoti wakhalitsa ku mpotoko kulima fodya. Izi ndi ma generational curses if these girls dont get delivered thier sons will also do the same to their daughters. The only way is Jesus who will break this yoke.

 19. DOPE IN SA says:

  LO MUNTHU YA BETA LO HAIBOOO. WATI INI? YOOOOOOO

 20. darius says:

  That’s the problem with you people who don’t come from northern province, you think all tumbuka speaking people are the same you are on the wrong side come to your before you comment.

 21. chejali says:

  Kkkkkkkkkk

 22. Nyauhango says:

  Anthu odziwa chigolo, ndife atumbuka, ndichifukwa chake mudzapeza kuti tonse ndi pachibale

 23. highlaw says:

  koma ya,,mahule onsewa,,kuuma eti!!!

 24. Anti wakwithu says:

  The reason this reporter did not reveal the name is to hide the tribe of this man, but we know he is a Gondwe, a core northerner. Northeners are the most virile tribe ever existed, their selfishness is beyond belief. Pamenepa samafuna wina adye anawo, koma adye yenkhe, they way they monopilize positions in offices. Agalu!!!!!!!!

 25. Critic eye says:

  Attumbuka mtundu wonyasa nkhope ndi mumtima momwe. Akuti ichi ndiye amachitcha mbiligha chija. Muzichita zimene konko and mukazachita zimenezi kuno kuchigawo chapakati kapena kumwera muzaziona. Mwina ameneyu si Harry uja ameneyu Mkanda…ire uja kkk kapena Thom Chi… kkk

 26. kholes says:

  Mulowoleso anao kuti mudziwanyenga bwino

 27. memory c says:

  It’s not about a tribe you fools. Why do u hate northerners? If u dont have anything to say just leave it to others. You sons and dotaz of vipers.

 28. Chosadziwa says:

  Atumbuka nyere ngati ya galu .mwana kumupweteka choncho. Mumawoneka ngati anthu ozindikira koma muli abulutu. Kungoti nkhuku imamwa dzira lake lomwe ndiye basi mwana wane dzakuno ndikunyenge. Imwe wadada mukasewenze basi zaka 43.

 29. AFANA ODANDAULA says:

  Atumbuka nyere ngati ya galu .mwana kumupweteka choncho. Mumawoneka ngati anthu ozindikira koma muli abulutu. Kungoti nkhuku imamwa dzira lake lomwe ndiye basi mwana wane dzakuno ndikunyenge. Imwe wadada mukasewenze basi zaka 43.

 30. Chosadziwa says:

  uwu ndiye mchitidwe wa AMBWENUMBWENU sizodabwisa ayi.

 31. Nyirendah Moo says:

  Since 2014 mumasiyilaji kukapanga report mafana inu/a neighbour since mutamva zimenezo have you ever warned of what his doing to his children inu mumaona ku police nkosangalasa eti pliz warn a person before he/she acts again

 32. Dr White says:

  Atumbuka ndi khalidwe lawo. Ukangokwatira nkazi wa chitumbuka abale ake aamuna akamafika nkumati alongosi alongosi atsiBweni basi uziwe kiti katundu akutha

 33. Kokotowa says:

  Za atumbuka izi ife zisatikhudze!

 34. jotchero lasatana says:

  mwanakazi mama wa mwana ali ko?

 35. ADE says:

  ANY PERSON WHO IS BRINGING TRIBAL ISSUE IN THIS SAD STORY IS AN IDIOT. THESE THINGS HAPPEN WORLD OVER AND IN EVERY DISTRICT, CULTURE IN MALAWI. SADLY SOME OF YOU ARE PRODUCTS OF INCESTUOUS RELATIONSHIP.

 36. Zowopsya says:

  where was the mother when this was happening. SOUND LIKE A BULL SHIT STORY. no offense nyasatimes.

 37. Nkulu ameneyi alibe maganizo a umunthu wenwen choncho ayera alandire chirang chokhwima kut ena atengelepo phunziro panchitidwe umeneu

 38. John M says:

  Ntchindere chakufikapo! Vizimba or vichi? He should be punished!!!!

 39. musa chilo says:

  anyongedwe atumbuka akuzolowera sivuto lina ayi koma mowa

 40. Kamkhwezule Kakang'ono says:

  Incest! At least if they were not biological children (step daughters)may be it can be understood. Was the mother an accomplice to the crime? Now what if he impregnated them? In all he should be sent to prison where his type belong.

 41. George says:

  Tachita manyazi tonse abambo. Uwu ndiye ndi ufiti weni weni n that idiot deserve to rot in Jail. Tiyeni tisamakhale ngati nkhuku umunthu uzititsusa

 42. Suicide Bonza says:

  Walakwa chani bamboo poti inu nomwe mumati ndi bwino anawa kuwauza tokha than aka phunzire kunja? Mdala amawa phunzitsa anawa kuti asadzakamu chititse manyazi kubanja. Ana adzi phunzirira mnyumba mwa makolo kumene!

 43. Winnie phiri says:

  Comment: akuti freedom yovala. What a nonsense! Amabungwenu apapa ndizowona kuti bamboyu walakwa kwambiri, komano yetsetsani kavalidwe ka wana atsikanawa kanyanya zedi. Zowona mawere, ntchafu padela akupita kwa atate awo. SHAME ON MALAWI.

  1. That’s bullshit winnie. Only a sick man would get horny for his daughter no matter how provocative her dressing

 44. Unknown says:

  Such a sick man

 45. muropwana says:

  I knew it was another northerner. The Mzuzu corner squad. Devils of the henga valley. Vindere vakufikapo.

 46. chalu says:

  What yimamwa madzila ake ipheni basi imeneyi

 47. Ziko likutha mpopano ana nawoso asinthe mukhalidwe wowonesa tnchafu pamutunda tipewe zimenezi kale kunalibe zimenezi and why today is common. Ana asikana kaya nyamata sitimalowa kuchipinda kwamakolo ife timalesedwa masiku ano mabele pamutunda mavalidwe onyenga malo obisika kumawonekera

 48. Tq of Zomba says:

  stupid bad father

 49. mphwanye says:

  Chindere chakufikapo! Shame!

 50. Lu An Li says:

  Comment
  Alya vipaso vyakhe. Ukazuzi nawo alije.

 51. Mkamwini says:

  Ana,kholo zitsilu zokhazokha

 52. Nkalapwaga says:

  Kula matunda yake lo!

 53. . . . . . . . . namweso
  . . . . . . . . wasungwana
  . . . . . . . . apa mutolepo
  . . . . . . . . chisambizgo
  . . . . . .. chakuti
  .. . . . . . . muleke
  . . . . . . . kuzgowezgana na
  . . . . .. . . awiskemwe
  . . . . . . . ngati ntchibwezi
  . . .. . .. . chako.

  ……….. chakuti
  ………. mumanye
  …….. awo nawo
  ……… mbanthu
  ………. nyele nawo
  ………yikufuka
  !………. 99% yanga

 54. Naxy says:

  CommentAmamwa madzira ake musiyeni!

 55. PHASKANI says:

  Chonde wadada imwe mukuchita ivo lekani kukoma wana winu. Wa police perekani chilango chakukhwima kwa wanthu awa kuti wamanye uheni ndipo kuti panji wangaleka kweniso chiwe chisambulizgo kuwanyake.

 56. Phaghlani Vwavwa says:

  The guy is not a Tumbuka. Shame on those with tribalistic attitudes towards other citizens

 57. pamsundu says:

  Comment
  Galu wa wagalu wose

 58. angelllina maliro says:

  oooh nooo

 59. edda mwalweni says:

  Atumbuka mudangova kuti mudzadya thukuta land , ndiye mpaka any obala wekha? Atumbuka mwandikwana ngati alhomwe, shame on you all. Ameneyo akakhale kundende moyo wake onse basi

 60. amfumu says:

  ngakhale nkhuku imamwa madzira ake, sindikuwonapo chovuta yapa katiyeni uko

 61. khriss chitsime says:

  winawu umakhala ndi ufiti kapena kugwima how can aman drink his own eggs

 62. that’s sodomy, last days

 63. kelvin says:

  Zopusa

 64. Chimdala chimenechi chikathanyulidwe ku ndende nachonso achichotse virginity. Mdala zimenezo zimakhala over protective. If you try to go out with their daughters zimakutulutsira agalu. Ku nyini kwako mbambo iwe. We will fuck your daughters while anyapala fuck you in the butt in jail. Chitsiru cha munthu.

 65. Cynthia Tamanda says:

  Ufiti

 66. Sangwani Mkandawire says:

  Please give him 20yrs nt 15yrs he is stupid chindele.mwana wong’ono kumamuika khosi lakolo mmesa khosilo amadziwa kuligwirisa ntchito ndi akadzi ako?

 67. Allan Mtonga says:

  Life inprisonment with hard labour is the right punishment for this stupid father.

 68. Denkhule says:

  Evil. The bible clearly reject such acts. He needs to be jailed but also recieve christ. Otherwise he will rot in jail and later end up in hell. Too bad for him.

 69. KUWILA CHILAMBO says:

  Chifukwa chiani nkhani za ntundu uwu zimachuluka ku mpoto? Paja atumbuka ndi opanda khalidwe, vindele va kufikapo.

 70. mwadia landwell says:

  Comment Imwe pala mwati phee mundayiwone nkhuku kumwa masumbu ghake. Dada uyu walya twake chonde

 71. matako a njoka says:

  yaaaahh! Atumbuka ngakhale ukwati amachita kuwapezera ndi makolo! zitsiru sizimatha kufusira iziii! kuda zili biiiiii

 72. benard riviel says:

  Kumwa madzira ake

 73. Tiyanjane says:

  Small minds talk about tribes. Big minds discuss issues and suggest solutions.

 74. johntembo Kuffor says:

  atumbuka ufiti nde nambala wani.

 75. charles says:

  uneneso wake ngwakuti kuli makola chidangire. chimunthu chamutundu uli? kuwenge kuno kwithu kwa kauma, lilongwe nga takoma waka kwambuya kuchema poli.

 76. Wanga says:

  Abale nsambi, azibambo munakhala bwanji ufiti? Timapensulo tanuto mkapya nato ku gehena. So l cant trust evn the father of my dota?

 77. Ishmael says:

  Atsikana nde mwabebatu mpaka kuilawa ya bambo anu kuyambira chaka chatha?
  Bas mwatha basi.Ndani akalakelake kudzagonana nanunso inu?
  Zaka 16 nkumalola kut mpaka Dad akuvuleni zoona?Mavuto ndithu!

 78. gwepenya says:

  ameneyo ndiye “wakwithu” Osadanda ngakhale nkhuku imamwa mazira ake.

 79. Atete says:

  Ana mukapita tnchafu pamtunda kuchipinda kwa atatewanu amanu kulibe mmafuna chani

 80. bongoman says:

  Chindere mwa vindere vose chikomani waka icho chilutenge kuchanya tamchanga kwenekuko

 81. GRACIAN KALIJE says:

  These people must be punished because its their resposibility to protect the children koma ndiwoso akumawononga anawa apa ndichimodzi kupha, mmmmmh koma amalawi ndichiyani kodi kapena kufuna kukhwima?

 82. yakweyakwe says:

  Ameneyo ndiye mtumbuka weniweni.kuopa kufunsira basi.ameneyo anyongedwe!!!!!!!!!!

 83. wawa says:

  kwao kwa Godal Gondwe kumeneko ndi khalidwe lawo

 84. Bamusi says:

  Kulaula dziko uku. Bongololo sawonetsa kwa mwana chonchi, manyaze bwa!!

 85. henz says:

  palibe zamtundu wa muthu apa alomwe ndi atumbuka zimachuluka kuti? Mupeza kuti ndalomwe ndi ayawo asiyeni atumbuka

 86. Anawo ndi vitsilu zenzene why not reporting the very first day

 87. boston nkaloh says:

  Nkhuku kumwa mazira ake! Kkkkkkkkkkk!

 88. sattoe felix says:

  Tili mmasiku otsiliza.Owerenga bible izi sizachilendo,yakwana nthawi kuti zobisika zonse zikhale pamtunda .Watsala winawe zako zatsala pang’ono kuti ziululuke.chenjera siya zoipazo usanayaluke.

 89. Kauzaneni says:

  This is bad, amangidwe kwambiri ameneyu!

 90. KARU UNITED says:

  Details provided by Mr A B Aliklyfi,appear to be convincing,this could end up being acts, perpetrated by an un documented illegal alien to the area (a tenant from elsewhere)

 91. Shonayi says:

  Atumbuka ndamenewotu.Azilamu awo ndiye sinkhani.Amachita kupereka dala .

 92. Comment chidada ntchindere chakufikapo ichi

 93. JOVANOVICH SCOTT says:

  amatamba ameneyu apite ku jere baxi.

 94. Titoh says:

  Koma nawe nde ukuona ngati ife tidzakwatila iwe utadyamo kale zachamba bwanj basi m’mangeni ameneyo asadzatulukeso a till anawo atadzalowa m’banja eet

 95. Lamulo ligwile ntchito mwaiye basi,osamusekelera.

 96. bamitutu wings. says:

  Nkhuku kumwa madzila ake hahahahaha what ashame!!!

 97. gogoda says:

  Eeeeeeeeee tumbuka man

 98. Atumbuka chigoloro pamodzi ndi akadzi omwe. Kumangoyenda mbolo ili pamtunda basi. Shame on you.

 99. charles says:

  Dada ndi zeleza uyu, wakukhukwa arrest

 100. osaweta jj says:

  Did u say unlawful sex with his daughter?does this mean that we have lawful sex with our daughters?clarify please

 101. Amos Magombo says:

  Dalayo alibe nzeru,kukhwima chani aphedwe basi asaononge tsogolo la Malawi ena atengelepo lesson

 102. pasipanadya says:

  Ufiti basi

 103. pasipanadya says:

  maliseche opaanda manyazi ngati awo sinawone

 104. Charles symon says:

  Ichi ndiye chamba chenicheni

 105. Western Cambriger says:

  Zochita za atumbuka, zimandisausa bwanji, tizingokhalira kumva za iwo

 106. C ufiti angakhale nkhuku imamwa mazila ake

 107. banyamulengi says:

  Atumbuka sianthu

 108. YOUNG WILZY says:

  go to hell !!!!!!!!!!!!!.

 109. Mr.Bambo says:

  Kodi nchiyani atumbuka?

 110. maganizo wa maganizo says:

  Bvuto la a Tumbuka ndi limenelo ndipo anthu amenewa akadzakhale pa okha ngat dziko la ku mpoto ana awo onse a kazi asamalire.

 111. Punchu says:

  koma bambo wotani uyu

 112. Mcherewatha says:

  Mtumbuka nde ameneyi!

 113. tiwonge says:

  Nkhuku yokumwa mazila ake.

 114. puludzu says:

  Masiku omaliza

 115. Mightwell says:

  14yrs yimeneyo why a child akulu alipo

 116. Kandakhute chinyetenyete says:

  Atumbuka phuma,anazionela kuukulu,mpaka mwana wako? Tulo,kuopa kufunsira akazi onsewa!!Ichi ndichindere chakufikapo chimangeni.

  1. kakarate says:

   Comment
   Ziakazi zinazinso zinaonongedwa kale zangokhala madzimadzi basi.

 117. HENGA MAN (Ma Fumu) says:

  A Tumbuka wanyane kukhwima panyake kusowa wanakazi? Chifukwa ivi mwachita apa mbuzeleza na uchindele Ukulu!!! Chiuta Wamulangani:

 118. point blank says:

  Examine this guy for insanity and he is of sound mind take him straight to maula prison. Sentence him to 2 life terms because he is inhuman.

 119. afere komweko kundende kukhwima kapena chani? ichi ndi chindere chakufikapo

 120. Agalu Pa Mpando[APM] says:

  Chimfiti chitsiru chikafere ku ndende.

 121. MAMINA says:

  MA BIZINESI A MBIRI PA MALAWI NDI WANTHU WOKHWIMIRA CHUMA

 122. charlie hebdo says:

  For the first time its not BALAKA!!! at centre stage. Men, when that thing is wishing, just go to the pubs and pay them alittle something…in this way, u will avoid untold suffering in your family and on your self.

 123. Wodzichepetsa says:

  Nde north imeneyo …no wonder last week yomweyi winaso amakwata sister wake

  lero bambo akukwata ana ake

  Atumbuka ndi a Lomwe chisembwere ndiye kudya kwao

  Ali ndi nyere za bulu

  kkkkkk

 124. billy wonjoya says:

  chinatota bwanji pakakuyaluka ndi ako omwe umafuna kukhwima chani

 125. Mazaza says:

  Mbachewa awa mwe wakwiza nankhalo zawuchindele kukaya pala wakulima foja tikuwonela waka wufipa kumaso kuti biiiiiii mbwe tamanya kuti awa mbamtundu

 126. agidy says:

  God have mercy

 127. chejali says:

  Ameneyu kwidzingani zenizeni or 40 yrs with ka rabour pang’no

 128. Kanka says;
  uwu ndiuzeleza chomeni,please uyo walangike.

 129. wamandasi says:

  Castrate all the rapists. Or cut their dicks and offer them rubber pipes to pee

 130. Gift Nyasulu says:

  Bwanji what is it with can he find something to do. May he get the right treatment for what he has done.

 131. Okhrana says:

  Eya atumbuka ndi choncho. Moti i have advised my 5 boy akazafuna kukwatira not atumbukan girl. Inu simumaona boys from tumbuka tribe amakwatira ku central and south nowdays akuwona wana kazi awo adada wawo wakugona mawo kkkkkk

 132. Kalizalizard says:

  Yamwa mazira akeee shaaaa!

 133. Wopondaponda says:

  Atumbuka bwanji kodi?

 134. chimbwititi says:

  chindele chachitumbukano .agalu inu

 135. BigMan says:

  And as usual, the mother probably knew all about it but kept quiet to save her marriage to this beast. shame!

 136. Apongozi says:

  Akufuna kukhwima chani?

 137. Kanjuchi says:

  Uli chindere mdala

 138. Maikolo says:

  Am not surprised atall, atumbuka ndi ntchito zao akuti nkhuku imamwa mazila ake omwe, hahahahahahaaaa!!

  1. kakarate says:

   Comment
   nkhuku imamwa mazira ake ndi chitumbuka?

 139. Gifted Brain says:

  Wawa a Tumbuka wawa?

 140. tsibweni says:

  cry my beloved nyasaland! dogs and pigs behave much much better.amangwetu, usavi chichi?

 141. tsibweni says:

  cry my beloved nyasaland!even dogs and pigs behave much much better.amangwetu, usavi chichi?

 142. MULHAKHO says:

  Uwo ndiye ufiti weniweni apasidwe 18 yrs in jailed zoba ameneyo.

 143. happening boy says:

  One has commented to Say the man os from Mulanje with a wife from Dowa, has lived in this area for 25years. Lomwe, chewa, citizenery tumbuka, three tribes involved. How coule thèse girls keep quiet all this while, Malawi Is coming to an end, sorry girls, Just get string and move on with your life, concetrate on school and overcome this trauma. Let the man face the law.

 144. Paul Vida says:

  Mwazuka bwanji atumbuka? Kukonda kuchinda basi.Comment

 145. Chitonombe says:

  Devil @ their best

 146. Adam nyangulu says:

  Uku ndie kusamuziwa mulungu munthu mumakhala ngati chinyama? izi zikumachitika mu dziko lonse lino osati kwa atumbuka kokha, achewa ndie mpaka mai anu omwe? Kukhwimira basi…….! Let the law take place.

 147. Nyamazikulu says:

  Why da dota reported late meaning she wz enjoy da game failing which she wud do it da vry 1st de so dat da law tke its course..

 148. Chosale says:

  Malawians have lost christian values and parental love. I fear the nation is going to the dogs. look how
  corrupt we are today. this man who has committed this serious offence can go scort free. watch out where the nation ia going.

 149. Eric mbamboo says:

  Uwu ndie ufiti weniweni.

  1. Macwaphee! says:

   Masiku omwe aneneri akhala akulalikira kut nthawi yomaliza,ndiimeneyi.

 150. Sandalasi says:

  No Sensible Comment Here. Malawians,make Relevant Comments And Those Full Of Educative Elements. No Baby Comments On Net Plz.

 151. Mbwiye says:

  Musamati aTumbuka, ena amakhala Ochewa olima fodya ku Mzimba. Iyaaaa! Khalidweli ndi lonyansa kaya wachita ndi mtumbuka kaya mlomwe! Ameneyo alandire chilango chokhwima basi.

 152. No tribelism if he has inhumanely treated her duaghters then let us seek justice. why behave like bokoharam miritants?

 153. costa phiri says:

  No problem paja mwambi wakulu umati khuku imamwa mandanda ake omwe

 154. The issue here is not Mntumbuka but an evil man who has been behaving like wild animal. Incest is a sin @ at the same time has made the life of his kids complicated cos that thing is gonna follow them the rest of their life

 155. Stupid daughters why reporting very late when ur stupid father started having sex with u a year ago?;(

 156. Malawianah says:

  Taboo..Very shameful n disgrace to our nation.He must rot in jail.

 157. Urunji says:

  Am sorry, this man is not a tumbuka but angoni. We the tumbukas are well mannered. Tingachita vya undere nga ivo ghaghi.We respect the norms and values bestowed upon by our ancestors including Themba la Mathemba Chikulamayembe–SABIRA

 158. Galu Wa Galu says:

  Nanga tilipilanso malowolo apa? Katundu adya kaleWADADA. KKKKKKKK.

 159. Bosho says:

  Atumbuka ndi dhilu kkkkkkk

 160. saiton Phiri says:

  Kufuna kulemela or chamba

 161. Enukweni says:

  This is bad, ma tenant ozalima fodyawa akuononga zina LA Atumbuka, Eni ake Ali phe.Azikalima kwina paja kuno ndi Ku mgodi eti but remember osabweretsa mkhalidwe wonyasa kuno kkkkkkk. T

 162. Koma aTumbuka uchitsilu, ine no wonder I hate this tribe, kuda too much

 163. Pedant says:

  Enukweni, Mzimba osati Enukwenu, Mzuzu.

 164. Boyoyo Boys says:

  Matsiku omaliza. (ameneyo si Mtumbuka koma ndi M’ngoni wakuMzimba) Mpachikeni basi.

 165. chikaiko says:

  Atumbuka mtundu wonukhatu ngati chipwisi chamazira achikuda,achinda ana awo akarha msikhu agalu mtundu owonukha ngati uwu kulibenso simudzalamulira ndinu makape nonse dzingochindani ana anuwo limero ndiye boma kupwanya chitanganya cha nyini za ana any ombeleka nokha fortseki zanu atumbubuka nyasi,

 166. Shimba says:

  amai ao muwakwere ana mwawabala nokha pokwerana muwathinikize mmesa atumbuka mitala imaloledwa kwatilani akazi ena awiri

 167. Malowolo mufunapo zingat-zingat?

 168. Yankees says:

  Nyasa kukanakhala ku Lomwe belt bwezi mutatchula Dzina la Munthuyo koma pakuti ndi Mtumbuka eh, mwabisa dzinalo why? Amwene tisanamizane palibe mtundu osachinda kapena ochinda kwambili as far as ndimunthu its Nature ndisadznveso mukukomenta kunena mtundu ayi, ngati Pitala boma lamukanika osati koma alomwe kuchinda nanga uyu ndimulomwe, oky tipange chonchi, Atumbuka kuphunzila? Bwanji pamenepo? Zitsilu!!

 169. Gwape says:

  wachita makola mganya uyo walwa masumbi ake omwe

 170. Anderson Benedict Alikyfi says:

  Do not rush into conclusions before knowing the identity of the culprit. I am based at Enukweni and I know the family vey well. The father is from Mulanje and works as tenant at Umoza estate. He married a woman from Dowa and have lived at this place for more than 25 years. Without pointing fingers at anyone. Let us remember that our tobacco estates are the epicenter of domestic and work abuse. Can government lift the lid of silence on these???

 171. Katakwe pa ndale says:

  Nkhuku ya njiru, kukonda kumwa mazira ake……cholinga? Mchitidwe ngati uwu uku kulirakulira…alandire chilango chokhwima kuti ena atengerepo phunziro

 172. matako m'mwamba says:

  Ameneyo ndiye mtumbuka ndikumuziwa ine. Ufiti komanso umbuli anthuwa

 173. Eddoh says:

  Unangali wena madala cbo choncho

 174. Thats crazy how can apot get into acup thats improper fraction,the man should face great penalties for that,thats inhuman.

 175. Anderson Benedict Alikyfi says:

  Do not rush into conclusions before knowing the identity of the culprit. I sm based

 176. bingiza says:

  I hate zomanena atumbuka this atumbuka that I have suffered enough xenophobia,soon tizingokhapanapo .zupusa

 177. Ronnie T says:

  Atumbuka eish mwawonjeza guys..Bola ife a chewa ndithu..

 178. isaac nkhata says:

  Dada ntchindere uyu

 179. ujeni says:

  who reads this anyway, online news should not give us this trash.

 180. Grey says:

  Kusowa umunthut kumeneko.

 181. Bololo Wachitumbuka says:

  Comment atumbuka kupanga chigololo ndi ana obeleka okha sizachilendo, zangolakwika kuti wagwidwa, mwanayonso poulula wa pwanya chikhalidwe cha makolo. Mark mai word wafumenge uko kundende

 182. njomba says:

  haaaa! Ameneyu simtumbuka ayi, ndi mlomwe ndithu. Koma wakhalitsa kwa a tumbuka basi.

 183. Ralph Kachindankhuku says:

  Atumbuka salemekeza girl child. To them girls are for sex or for selling and exchane with cows.

 184. Siphire says:

  Ufiti sungapose umenewo

 185. T/A says:

  Amati mtundu wagwiro ache aniyikewo amatero,

 186. Mtambo says:

  Comment…wachita bamboyi ndi ndikupha,apatsidwe chirango chonkwima kuti ena atengepo phuziro.

 187. wagwanayo says:

  How come this only happens in Tumbukaland? Please you people must change behaviour.

 188. masoankhono says:

  nyasi ! atumbukawa akuchulukisa nchitidwe wanyasiwu. mpaseni chilango chokhwima ena aphunzire.

 189. pontesi says:

  mwatilaula madala , ufiti basi

Comments are closed.