Email a copy of 'Father asks Red Lions to cheer his son still in comma after Malawi football violence' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

75 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
NEEMA
NEEMA
8 years ago

Mpititseni kunja mwana wa munthu Bongo usanawonongeke chondee mwee!

kholes
8 years ago

Palibeso chifukwa choti asilikali adzibwelera kuchipatala koma kupeza treatment kunja kwamalawi kuti mwanao akhale mmene analili.kapena matimu asilikali amenyene ndalama zapageti apantse mwanao apitile ku India akalandile treatmenta.

Mr.Bambo
Mr.Bambo
8 years ago

@ 24 years still staying with mum and dad?

Mphangela
Mphangela
8 years ago

Vuto la kuno ku malawi asilikali amadzitenga opambana kuposa aliyense ,a sulom kodi super leage singayende mutachotsa matimu achisilikaliwa?chifukwa chaka chilichose kuma game oti yina ikusewera ndi matimu asilikali kumakonda kukhala ziwawa osangowachotsa bwanji akhale ndi zawo ku ma baracks. kwawoko. Komaso anduna mnyamatayu mutumizeni zipatala za kunja ma bill akalipila a red lions si omwe amupatsa vuto munthuyu.pangani zoti achile otherwise aliyense anakhudzako pomenya mnyamatayu ur days r numberd.

Man rich
Man rich
8 years ago

Agalu amenewa ayiwal kuti akudya misonkho yathu,akatiphamo atawalipile di ndani.vuto ndi lotenga asilikali osaphunzila,mitu zani.matimu onse a chisilikali asiye kusewela mpira.

Joe Nkhata
Joe Nkhata
8 years ago

It’s true Tamala Mauwa akunena zoona

mikes
8 years ago

the sodiers who wer involved beating the man , i swear the terible troubles ar upon dem

Gerard Banda
Gerard Banda
8 years ago

A Sulom chotsani Red Lions mu Supper League and also ban asilikali onse a ku Chichiri camp from watching football otherwise ine zikundiwawa kwambiri,raising a child for 24 years is not a joke,asilikali a kuno kusowa chochita nchifukwa chake akumavulaza anthu chonchi,ntchito yake iti mukunyadila inu

blessings osama chidakwani

Soldiers are meant to protect its citizens not the other way round..kumalawi chinakula ndi umbuli..most cases asilikali Amakhala busy kulimbana ndi defenceless Pple which is not the case in some countries!! Soldiers like those need to be taught a bit lesson….am warning yu,if yu try to do this kind of shit to one of my family member,i will fight yu with all I have…Malawian soldiers are a disgrace

mtichimwitsa
mtichimwitsa
8 years ago

Wins ndimulodza akapanda kuchira ndikudziwa yamanja mundipweteka mxiiii agalu inu

Read previous post:
This is Malawi, are you surprised? – Lawyer John Gift Makhwawa

I grew up reading magazines. Two if not three or four of them. But I liked one and only one....

Close