Email a copy of 'FDH Bank in fresh contempt of court for advertising to sale Maranatha Girls Academy' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'FDH Bank in fresh contempt of court for advertising to sale Maranatha Girls Academy' to a friend
Main opposition Malawi Congress Party (MCP) president Lazarus Chakwera has called for party unity, saying the problems rocking the oldest...
tinakubelani bank zankutu Mumthu amapela ndalama ukamaba we paid alot of money . Inu bwanji simunagule anailengeza mnyuzi akutumani ndani .nzanuyo wazisekela mwayi
Kkkkkk mbuzi zokhazokha u ha got a case to answer going ku maranatha kukawasegulila ana akusamba cholinga chanu chinali chani poti mumatchuka ndizotamba kapena mumafuna kukhwima chifukwa zinazo sizikumveka khoti inalesa
Chosamva achiphikira mmasamba muchiona. Chimva nkhwangwa ili mmutu. Chikadadekha chikadaona nkhasako. Madzi afika mkhosi. Ngati chili chinyengo, diso lipenya. Nkhanga ziona kumwezi. Ukauma ntima Choipa chimatsata mwini. Ukakhala mmwamba usanyoze pansi.
Approach clients professionally and win more of them and avoid losing business because of arrogance
Ndawelenga macomment onse it seams amalawi mwazindikila zija ndimati Malawian banks are not there not to help u grow but finish u .Maranatha azinkhala wosachangamukako which is not the case with more Malawian anatha apa. Look the banks according to assessment they are to pay him more than what the bank is claiming. Bank yomweyo ikukanika kupereka 800million kumaratha koma ati ikugulisa school chifukwa ikufuna 400million no logic and it doesn’t make osangochosako yawoyo ndikusayisokoneza school and anzanu nawo aphunzire ngati momwe munaphunzilila inu. Malawian banks change please,many people are in trouble because of this tendency we know u have… Read more »
Palibe nkhani apa kungoti aguluwa akumana amatama zinthu zimatha ndi kukambirana sakuziwa akuonongelana business,mabank ene akukondwa ndi izi komaso maschool akukondwa so watch out
Anthu andalama amadelela pakufunika amagidwe kuti aziwi money can’t save them
Banks officials going into girls bathroom and and toilets .what was intention after being saved with injunction restraining them to sale. Is it because they have more money to buy judges and more lawyers or because this bank is close to APM . But now is above the law ,chilungamo chiyende ngati madzi We thank the high court for ur vivid stand and summoning them to answer contempt.
U mean that bank goes that low why work up guys banks are supposed to stable, sober and mature
Bank ya FDH ndiyausilu yimasata mmapazi macustomers ake anthu ambiri akuidandala yachuluka zibwana, No wonder l bank with Nb
It’s the that say fdh yalakwa if I got your question right. Contempt of court orders means one has not complied or obeyed what court has ordered or instructed one to do or not to do. it is the court of malawi with all the authority and mandate to provide a service of. arbitration in malawi according to our Malawian costitition. Of course we are all entitled to our own opinions as individuals but the court has a final say authoritatively. So the court will determine what’s next for these fdh bank so called bosses after the court hearing. No… Read more »