Email a copy of 'Footballer Mlimbika marries his sweetheart' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Footballer Mlimbika marries his sweetheart' to a friend
Battle for points in the in the OG Issa Southern Region Netball League (SRNL)continues to get tougher every week as...
Wapeza m’kazi wapeza chithu chabwino pano muzimenya m’pira m’tima uli m’malo kuti kudeni wasiyako madam zithu zabwino
Enanu mumangodziwa kunena azanu inu zikukukanikani pepani
Congrants.
WAPEZA MKAZI WAPEZA CHITHU CHABWINO
Ndikukufunirani banja lopambana ndilachisangalaro, Ngakhale malemba akunena kuti awiri aposa mmodzi.Sichinthu chapafupi kupeza omukonda chifukwa zachuluka lerozi ndizachinyengo.
Ukwati mkutchalichi inde koma pamafunika kukonza kuti zithunzi mukamazaziona ayi kumati yaah, thst was my big day. Apa zikuoneka kuti munangodzuka kuti tiyeni tikadalitse not bad.
Natural hairs Tendai mukana trimer mkupesa bobo. Pano naturals inde ili mu fashion but iyi ndoya mu 19 gobede.
Amunawo abale, munangochokelavku training kapena basi mumvekele Tendai sita shirt iyi.
Mwanayo abale mmutumo, blue, pink and white. Azakudandaulanitu chifukwa anzake angaseke.
Other than that ayi ndithu mwachitabwino. Zikomo kumpando.
mkaxi uyu mwamukwatiladi,mmmmh
Zoona wachita bwino osamangovula ana ayeeniake mkuthana nawo
Family life is very important especially public figure ena amangozipeleka kuti chilichonse mutafune ndikupatsa bola kutchuka
After fews days wapitanso kwa wina those girls will not get married
Big-up francis
No 22,ukulimbana ndikunyoza munthu coz sumatsatira team yomwe amamenya?uli ndichani vumbwe ngati iwe
pangisani wanu msamangonena anzanu.