Kodi a dickson munakanika kumunyamula nkaziyo? Ndamva kuti munkafuna kumugwesa kkkkkkkk anyway first month muzidya nsima yamgaiwa mutolele mphavu
All the best bro mwaitha
Mwaitha a DCG. Enanu ndi nsanje chabe paja kuyamika kwaenanu ndimwikho
mwana mulopwana
8 years ago
The most important thing is that the guy made his vows , the issue of dressing does not matter at all even if he had dressed like a football prayer during his wedding, we waist our time in trivial things leaving behind the important things,
Zonyadisa achivwati
inde nyasatimes osazaiwala kutiuzanso mkaziyo akayamba kunyengetsa kumbali…komanso mamunayo akayamba kumuswa makofi mkaziyo muzalembenso pompa mwina kuikanso pictorial focus…si mwayamba chonchi?
NKAZIYONSO SANAMETE KU NKHWAPA
Vyi kunowa
muziyenda kumaona momwe anzanu amatchenera mmaukwati, decoration yonsansa, dressing poor hmmm
Kodi a dickson munakanika kumunyamula nkaziyo? Ndamva kuti munkafuna kumugwesa kkkkkkkk anyway first month muzidya nsima yamgaiwa mutolele mphavu
All the best bro mwaitha
“We Waist time” I understand You meant to say “WASTE” .Nice comments my friend but use your spell checker professionally. Keep it up.
kumathandizana atola nkhani ndi zofunika