Email a copy of 'George Nyirenda rejoins Bullets from Caps of Zimbabwe' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'George Nyirenda rejoins Bullets from Caps of Zimbabwe' to a friend
For the first time in the history of St Anthony’s Kachebere Major Seminary of the Catholic Church under the Episcopal...
UR MOST WELCOM
Ok george koma dont revise what you did to mapalestina
Bullets! Bullets! Bullets! Bullets ndi moto. Neba ndathokoza kuti dzuro wawina kumatero tisamakusiye mamitre mpaka mwakuti ngati enawa. Bwanji kodi? George disciplin ikufunika osamatisiya mwendo uli mmwamba. Ku Malawi kuti paliponse nkhani ndi ya Bullets mwinanso Mugabe Gabriel Robert munamumva akuti “noyenda mu Africa but BuLlets inonesa iri sitereki maningi.” Amanena Bullets yake yomweyi!
a Jon Gondwe pangani zanu asat za Nyere nsanje tipange ndi ndani muzakhumudwa titatenga superleague its not over until it is over.usapota wanu usakhale ngat wa Chakwera opposition.Ma timu pa Malawi ndi awiri yanuyo ndi noma.ndichifukwa dabe ija siliva ndi noma imalowamo katatu.
Welcome back George Koma pliz machokedwe azikhala abwino look today u r at bullets we have welcomed u.
Welcome back geo
Welcome back Geoge Nyirenda
A Tewesa Which George Nyirenda is coming back to BB? I have meant him at Mwanza heading to Zimbabwe.Koma Tewesa ?Let me wait to see him back in Red and White.
Welcome G. Nyirenda, timakunyadira……..takufira heavy!
wachita bwino geo feel free your a brilliance defender,we proud of you.