Email a copy of 'Great Angels Choir offers fans Christmas bonus in Mwasankha Ine DVD' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Nabanda
Nabanda
8 years ago

go konko, amadelera….mukaimbeko udelanji nkhawa, ilike that song sooomuch,,imndisuntha.

Francisco
Francisco
8 years ago

Nanga kuno ku Mangochi, bwanji osabwera?

Koma ?????
Koma ?????
8 years ago

Zonda, where can we buy the DVDs?
There are some people who can not patronise these places…can you think of some shows in places like Capital Hotel, BICC.. even if its 3000 or more per head, there is still a category of people that can attend such shows…just free advise for your marketing section!

Jerejede
Jerejede
8 years ago

Great Angels!!!!!!!!!!Woooooooooh

Enock Gideon
8 years ago

kupatula malo omwe munazolowela kupanga show yendaniso mmalo omwe ukufunika uthenga koma malowo ankale akumuzi monga Luchenza, Thondwe, Thambani, Mayaka ndi malo ena omwe sanakuoneni chiyambire kuyimba nyimbo zanu zabwinozo. Mulungu akuyitanilani ku ntchito yake maka kwa omwe sakunziwa Mulungu. Ndisiyeni ndiyende, Mwasankha ine, Wakuimilira ndani? ndi zina zambiri ndi nyimbo zomwe ndimakonda ammmmmeeeeeeeeen!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

Rodwell malunga
Rodwell malunga
8 years ago

ndidzabwera m’ma 4am muzandipeza nditafika kale eeeeeeee

Collider Simwaba
Collider Simwaba
8 years ago

Nanga ifenso kuno ku Blantyre Robins Park mubwere pa 31st December, 2015 tikufuna kutsitsimuka, tikamamva nyimbo zanu mabvuto onse amatha. Amen!

jona mtowa
jona mtowa
8 years ago

Nanga kuno ku Zomba abale. Kungotisiya osadalitsika

opportunist
opportunist
8 years ago

Kumeneku kukavuta.

Read previous post:
tH
I’m not tainted with Cashgate, Kamlepo seeks apology from Minister Nankhumwa

Rumphi east MP Kamlepo Kalua has asked Local Government minister Kondwani Nankhumwa to apologise to him for allegedly linking him...

Close