Email a copy of '‘Hardcore criminals’ Mvula and Gombwa get bail' to a friend
Loading ...
Email a copy of '‘Hardcore criminals’ Mvula and Gombwa get bail' to a friend
The Institute of Chartered Accountants in Malawi (ICAM) has hiked Hennox Mazengera Financial Reporting Award from K1.2million to K1.5million. ICAM...
Jack my Friend this is Laughable Very Laughable….Kikikikikikikik ukungokhalangati Dausi &His friends….find out where there are as of Yesteday &Come back &write ur Bullshit…..chaka Mawoneka Anthu Opusa,with No Brains,Sukulu,…..My word!!!!!!!!!!!… just Because you have your Theories & u think Are right????????????……PPle Here have Become judge &jury over this story its not Fair to both gentlemen (Mvula&Gombwa) Mark Words I REPEAT Mark MY WORDS They are going to Walk. They Will Walk out This Situation that there Are in…Not Because of their Status or their Money Because Its the Truth…….A Malawi Ndinu Anthu AvesaChisoni. Kubwetuka Ndikhani…….omwe Anaphawo Alipo ndiposo akuvomera sakukana… Read more »
a Jack poti a Dumisani wo is still in Prison ndiye munamizira ndani kupepela basi , pitani lero ku Chichiri mukamupeza Gombwa ndi Dumisani… mukanakhala kuti mumadziwa kwambiri zamalamulo mukanadziwa kuti anthuwa sakanapita pa bail lolemba lomwelo..Kusauka a jack ndi maganizo omwe zoona eeehhh
I agree with number 9. Dumisani Mvula akungomunamizila, we know the story kungoti a police akupezerapo mwayi cos his gfather is not strong nowadays. His friends used his fon, kodi inu anzanu akafuna kuyimba fon simumawabwereka? Angakuuzeni kuti akuyimbila kuti? We all know kuti a police athu are trying to cover their fellow policemen who were involved in this nde popeza ukakhala mu cell umakhala wopandq voice nkona akuyankhula momwe angathere. Koma am telling u these boys are innocent. Amaphawo anali a police. Bwanji that policeman ankati anatenga mfuti ya boma wati zii sakumutchulanso. Wake up Malawi
A Jack nanu musawonjezere gaga mdiwa, nde kuti kukamabedwa ku area imeneyi ndi anawa basi? A Police akuwabisa anzawo omwe amaba limodzi ndi anawa…. akuwanamizila. Mark my words.
After being released,yesterday there was a daylight attempt to rob in Chigumula but,the thieves found Cheques only not cash and the robbers killed the assistant to the driver,the minibus used by robbers never reached Limbe,its within the area and Mvula stays in BCA,I hope police will investigate properly
mbavazo zisapasidwe bail .afiiti amenewo
mild
Mukawawona asambitseni ndi petrol Mukawawona
pa town.
its very absurd to release. such people on bail. They initiary admitted but later denied. Judicial should leave such cases to police.
mwati muthana nawo eti? angokuomberanipo za ziiii kkkkk sima water gun awa
Lol mbava ziti? Zinakuberani chani? Ndipo anagamula kuti ndiokuba ndani? Ndipo evidence yanu ili kuti yomwe itionetsa kuti ndiokuba; ilikuti? Basi yabeba ndi slander and defamation? Ntchito yaapolice ndikufufuza pena amalakwisa pena amapanga zotheka pena ayi. Kumangidwa sikutanthauza kuti walakwisa ndi ma court amene alindi mau otsiriza ndipo nthawizina ma court amalakwisa. Umunthu wanu uli kuti? Kumangolemba zinthu ngati ndizoona koma zinthu akufufuzabe? Anthuwa anakulakwirani chani? Mukati ndi ana a anthu olemera iwo anasankha kuti azibambo awo akhale amenewo? Si Mulungu amene anawa sankhira, monga Mulungu sanatisankhire tonse? aMalawi tinakhala bwanji? Olo muwanene zotani ngati sanalakwise sanalakwise. Za padziko izi,… Read more »