Email a copy of 'Head teacher sexually assault 14-year-old pupil in Mangochi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Head teacher sexually assault 14-year-old pupil in Mangochi' to a friend
Delick Chiwala, 49, working as a security guard at Sosi Lodge in Lilongwe is not reporting for duties because he...
55yrs-14Yyrs….Mmmmh,Yalakwa.
more fire south
Ana a chawa kudelera paja amati mwamuna samapha
wnawonso ayawo ndi achina amberechile kumtumbo kwangali ngöngole mwina kanatenga mapensulo wa ahead?
Tiziti Azibambo ozerezeka ndi chigololo ali kumwera eti?zamanyazitu izi abale.ena timagalimoto tawo,kumachita kuika ka tintedi chifukwa chokuti atonyamula kamwana ka saizi ya mwanawo,kumanamizira kuti akayesa mwanawo sanapite ku sukulu,kuli kufuna kupweteka mwana wa nzawo.
Taganizirani ali wanu mwana,atatengana ndi mchidala ngati inu bwaa? akulirenji bvumbwe otsakamira pa ka tsekera kang’onong’ono.kuti muone zambiri amalawi anzanga,muzitchera pa lanchi,enanu mudzakhumudwa.akunamiza anchito pakhomo kuti mzake wa mwana wanga.timatoyaluka ife amene timatoziona ndi maso.
Tiziti Azibambo ozerezeka ndi chigololo ali kumwera eti?zamanyazitu izi abale.ena timagalimoto tawo,kumachita kuika ka tintedi chifukwa chokuti atonyamula kamwana ka saizi ya mwanawo,kumanamizira kuti akayesa mwanawo sanapite ku sukulu,kuli kufuna kupweteka mwana wa nzawo.
Taganizirani ali wanu mwana,atatengana ndi mchidala ngati inu bwaa? akulirenji bvumbwe otsakamira pa ka tsekera kang’onong’ono.kuti muone zambiri amalawi anzanga,muzitchera pa lanchi,enanu mudzakhumudwa.akunamiza anchito pakhomo kuti mzake wa mwana wanga.timatoyaluka ife amene timatozina ndi maso.
Boko Haram yonseyi mpaka kamwana kakang’ono.kodi azibambo oterewa sachita manyazi,akamavurila tiana ta saizi ya ana awo?
Ambuye nthawi yatha bwerani mudzaweluze dzikoli
Peat coat ndi chaninso abale? It’s “petticoat”
WAONJEZA WAKOZERA TIKITI